Zomwe mwapanga a Mcp Ku Parliament ndi zachimidzi zaugalu ife sitiopa kutimanga, Hot Current yachema

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 дек 2024

Комментарии • 44

  • @DaeyangSonon
    @DaeyangSonon 5 часов назад +7

    APM anapanga ubale ndi North Korea, to counter threat ya Tanzania, zabwera nyau nkungoti basi tengani nyanja

  • @GidionLufani
    @GidionLufani 6 часов назад +7

    Angobweletsa black box ndiye imene ilindiumboni

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 6 часов назад +5

    Welcome madoda watching Live from Pretoria SA

  • @FannyTaibu
    @FannyTaibu 6 часов назад +4

    More 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 from Zambia

  • @modestamhango7737
    @modestamhango7737 3 часа назад

    Ku Malawi anthu amafa ndi matenda ochizika chifukwa chosowa chithandizo mchipatala. 😭😭

  • @kennymwanyongo8165
    @kennymwanyongo8165 5 часов назад +2

    You're all missing the point.
    All answers on a Plane crash are resolved by accessing information from the Black Box.
    The question is; WHERE IS IT and WHY!!?

  • @officialturfrican_ent
    @officialturfrican_ent 4 часа назад +1

    Watching from south America

  • @LinessPelete
    @LinessPelete 5 часов назад +1

    President wathu adapita ndipo mukamakambabe za ndegezi zikutiwawa kwambiri Kuli bwino mungosiya kuyankhula zimenezo palibe yankho lomveka limene lingayankhe Mayankho a imfa ya SKC

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 6 часов назад +2

    Tikufuna ma fighter jet kuti tithane ndi mzimayi wa ku Tanzania

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr 5 часов назад +2

    Dpp weye kuno ku NU

  • @BactonJasten
    @BactonJasten 3 часа назад

    Where is black box kodi enquiry sinafufuze😢😢

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 5 часов назад +2

    That accident was planned a lot of people were involved .Lets talk zaku Tanzania 🇹🇿 tsopano that woman she wants to take lake Malawi

  • @HaroldBornface-o7p
    @HaroldBornface-o7p Час назад

    Airport kukhala ngati pa new Shire area49 chonde tiyeni tilikonde dziko lathu momwe timakondera ana athu powatumiza ku school zodhula zija timawalipira muja ngakhale muwatumize ku UK koma ID yawo ndi akumalawi basi please

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 6 часов назад +2

    Apatu mufufuze nthawi ya Bingu zinayenda bwanji? Apa kumalimbikira chifukwa chipani chani cha DPP sichinatchulidwe eti?

  • @GidionLufani
    @GidionLufani 6 часов назад +2

    Zosezo zonama amafuna chilima aphedwe .oyendettsa denge sanalakwitse ay I akumunamizila chifukwa chapati anafa sangayakhule

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 6 часов назад +1

    Palibe chomwe chinalondoledwa pa searching ya ndege kuyamba kunyamka kwa ndege from lilongwe airport nyengo singasinthe in a brink of eye so everything was totally mess

  • @HaroldBornface-o7p
    @HaroldBornface-o7p Час назад

    😂😂😂😂😂chilungamo chimawawa koma ma guy awa amayankhula dzoona ndithu koma ukamanvera muchi boma ndilomweli umanva ngati akunena iweyo 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅koma ineyo ndimagura bundle chifukwa Cha hot iyiyi 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 3 часа назад

    Mmene mwanenela za afrobometer ma figawa zikuonesabe kuti dpp idakali ndi mwayi chifukwa cakuti kumwela 70% kale, pakatinso pali dpp, kumpoto panopa kuli dpp komanso utm ndi aford nde mukhoza kuona kuti APM ali ndi mwayi onse otenga boma cifukwa dzigawo zonse za dziko lino APM ali mkamwa mkamwa.kumpoto ndikumwela mcp isawelengele kulibe chawo awa adzavoteledwa ndi nyau zawo zomwezo mcp mbuzi za anthu.

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 5 часов назад

    Chakwera ndi boma lake la Mcp akuzunzadi a Malawi omwe anapuma ntchito posawapasa ndalama zawo please tiyeni tizikhala ndi umunthu

  • @giftkayome3568
    @giftkayome3568 4 часа назад

    Ndalama zimathera mmatumba mwawo tisalira mumbuyo mpaka muyaya

  • @HawaHussein-o5k
    @HawaHussein-o5k 5 часов назад

    Mchifukwa chani anachedwa kukapanga search komaso mkuletsa kuti kwada?

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 4 часа назад

    Ndegeinalibe vuto ndege anachitatu kugwetsa

  • @SteveKanongwa
    @SteveKanongwa 5 часов назад +1

    Hot currency ingonena kuti dpp ndimene izawine

  • @DumiMhango
    @DumiMhango 18 минут назад

    Anzathu achewa awa ambili chimizi chidapweteka nchifukwa ambili amaiwala or kusamba

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 4 часа назад +1

    Inu musiye nyasi zanu zochita comment nkhani ya ndege, chifukwa Chilima anachita kuphedwa ndiye kukadzabwera kafukufuku wina mudzachita comment chiani.

  • @elisawittika9385
    @elisawittika9385 5 часов назад +1

    We can do better

  • @RichardNgomba
    @RichardNgomba 6 часов назад +2

    Awa anabwera

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr 5 часов назад

    Central region ndiyo gawanika MCP ichenele ineyo ndiwaku central konkuno sizilibwino pa ground

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 5 часов назад +1

    Do not use that rubbish report for your comments. That is a fake report just like the Chizuma one. That lady was a good pilot, She has been flying the aeroplane without a problem. Nkhani apa ndi yakupha Chilima. How good a pilot can be but if is misguided through technology there is nothing a pilot can do to avoid such man made accident. Please do not blame the pilot just because is dead and can not answer for herself, this is not good at all.

  • @HandEllah
    @HandEllah 6 часов назад +2

    😂😂😂 Koma kwavuta

  • @FelixMachika
    @FelixMachika 6 часов назад

    Mavuto atikwana kale, kuyankhula kwa Bwanji uku Jonah? 😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 6 часов назад +1

    Kodi nkhani yanyanjayi ikuyenda bwanji chifukwatu image sitiiwala msanga ngati mmene amachitira a Times .2014 campaign ya Peter Muthalika yogonjetsera Joyce Banda inali yakuti akangosankhidwa Peter Muthalika choyambirira apanga za nyanja. Atasankhidwa sanapitenso kuti akakambe za nyanja.Apa nkhani ija yatulukiranso. Ndiye poti Andale amationera apanso ayiwakha nkhaniyi kuyiyika pa Top pa campaign zitsiru zomwe zimaomba mmanja 2014 panonso Zomba mmanja. Pofunika Peter yu kumafunsa paja munanama zanyanja pano ziii pati? Chifukwatu nyanja ndiye aigawana.

    • @FWhite-w3l
      @FWhite-w3l 5 часов назад

      Vuto ma president akumalawi amangofuna kulemera dziko ndikumasauka zakumachende

  • @HawaHussein-o5k
    @HawaHussein-o5k 5 часов назад +1

    Manga black box ilikuti kuti ifotokoze zoona

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  4 часа назад

      @@HawaHussein-o5k Za black box sakukambaditu

  • @Josephiriillovo
    @Josephiriillovo 5 часов назад

    We can do better kuti galu iwe nkhani inali yokupha skc basi

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 6 часов назад

    awuzeni angonyera utchi tawina ngati kt anthu amvota kale akuti kudalira kuba tinyesanatu 2025

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 6 часов назад +1

    Inuyo a times since ngoziyi itachitika you were in government side so it's not a strange kuti lero mli pano telling malawian kuti agwilizane ndi manyaka anuwa zisiike plan crushe was planned thing nothing much

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 4 часа назад

      Zoona, anthu amenewa akutinyasa ndi macomment a ndege. Chifukwa Chilima anachita kuphedwa ndi Chakwera

  • @kantayeniphiri4016
    @kantayeniphiri4016 6 часов назад

    Koma pa you tube pa nde paphweka ndi ndale za ku Malawi...

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 6 часов назад

    Kodi za nyanja yomwe agurisa niyambari yakuti yakusongeya or yakuti tiziwe

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 6 часов назад

    Misewu ya ku chitipa mumayendaso nkhalamba,muma bump momwemo nde how special are these nkhalamba you are talking about anaganizilapo kuti ku chitipako kukufinika misewu ? Asamapiteko if they think akumadusa misewu ya kumeneko mumangodutsa nyama za ku tchire.

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 6 часов назад

    Without being able to Account for this money this is a CARTEL stealing our money. We pay a gang expecting nothing in return just to live in Malawi.