Zoona pastor Mbewe akulephera kutsutsa koma akufuna kudzalamulira.chiyembekezero cha anthu ndichotani kwa anthu ngati amenewa.Boma la MCP likutizuza.ndalama zikupezeka ndizoyendera maulendo ake.ndipo mkazi wa Chakwera ndi galu.mzimayi wathundu wanji olephera kudzudzula mamuna wake kuti bambo anthu akuvutika uku.
Prophet Mbewe you're right about opposition and what I can see here is that Malawi has no opposition leader and because of weak APM that's why all these things are happening if it was Bakili or late Bingu this wouldn't happened
This is so true,,,if they are wise enough let them start now,,,it's high time our leaders start seeing this nation that it is for all of us the government and the opposition
God is very Merciful and All_Knower. Almighty God knew that in fact there are no opposition parties in Malawi, then God has brought the hope for poor Malawians hon. Bon Kalindo, the president of the poor Malawians. This is shown by the way the called opposition parties in Malawi are silent while nothing is working in Malawi. Only hon. Bon Kalindo is condemning this bad leadership. May Almighty God bless our president Bon Kalindo and his comrades with long live and strength against the devils sent to destroy our peaceful and beautiful country, Malawi.
Especially Nankhumwa is busy fighting with APM and he think like it's easy to be a President of Malawi while people are dying with hunger in the hands of Chakwera.
It will be a very big mistake for people to vote for Nankumwa as a presidential candidate and he's not supposed even to be called Vice President of DPP. That's why DPP will have no future and it's shameful for the party that was strong to finish like that because of selfish people like this
Koma zokuti mudziko lamalawi zinthu zikusokonera chifukwa opposition leader ikufooka idzo ndiye zoona opposition iri mbali ya m c p osati anthu ndiye.kusogoloku adzitisokosa muvotere nankhumwa tidziti ndizolondola ?pomwe asakuyimira osauka .😂😂😂😂
How can DPP oppose the government that the citizens chose to the best of their knowledge. The citizens said DPP was worse than mcp how then DPP can oppose what the citizens chose as best. Don't accuse DPP because of your wrong casting of your vote, don't push DPP to clean the mess you created on your own, be the solution to your political mess
Amen papa😍😍😍😍😍
Powerful saying man of God.....
Video iyiyi ikamupedze Nakhumwa,,, straight point
Amen
May God bless you
Zoona pastor Mbewe akulephera kutsutsa koma akufuna kudzalamulira.chiyembekezero cha anthu ndichotani kwa anthu ngati amenewa.Boma la MCP likutizuza.ndalama zikupezeka ndizoyendera maulendo ake.ndipo mkazi wa Chakwera ndi galu.mzimayi wathundu wanji olephera kudzudzula mamuna wake kuti bambo anthu akuvutika uku.
Very very true Man of God
Prophert Mbewe .izi ndizona zikhazokha anthu mumalawi muno akuvutika kowophya
malawi alipamoto .kuiguptonso pangono .Mulungu ayendere malawi.Mbava sitikuzifuna .usogoleri wazuza anthu uwu
I agree he is right.
This is true,
Opposition Mps and leader of Opposition ali weak kwambili, akungoganiza zautsogoleri
You are a great person
The dude is spilling the facts
Prophet Mbewe you're right about opposition and what I can see here is that Malawi has no opposition leader and because of weak APM that's why all these things are happening if it was Bakili or late Bingu this wouldn't happened
True mr prophet , here in malawi we don't have opposition parties , all of them ndi adyela, even pac nayonso inalowa mbwelela
Ndagwilizana nanu prophet
This is so true,,,if they are wise enough let them start now,,,it's high time our leaders start seeing this nation that it is for all of us the government and the opposition
God is very Merciful and All_Knower. Almighty God knew that in fact there are no opposition parties in Malawi, then God has brought the hope for poor Malawians hon. Bon Kalindo, the president of the poor Malawians. This is shown by the way the called opposition parties in Malawi are silent while nothing is working in Malawi. Only hon. Bon Kalindo is condemning this bad leadership. May Almighty God bless our president Bon Kalindo and his comrades with long live and strength against the devils sent to destroy our peaceful and beautiful country, Malawi.
They must show leadership now like this dude kalindo
Amen
I wish Born Kalindo azatiimilire u president 2025
🤣🤣🤣🤣
Powerful
Good advice sir
powerful message
I don't agree
Munthu uyu wayankhula chilungamo@@fosterkatemba1269
This reall prophet David mbewe what he said it's true
I agree
Great
Exactly MoG
He is right
Especially Nankhumwa is busy fighting with APM and he think like it's easy to be a President of Malawi while people are dying with hunger in the hands of Chakwera.
Ndale zapamalawi anthu akutaya nazo mulungu kusatila mdale nconco mulungu akakwiya mudziyankhula zambiri inu anthu odziwa mau amulumgu nanga mukuphatikizilanji ndizachikumja inu ndiye musintha zinthu analipo anzanutu alipo lerowa amayenda bawo kudya usipa pamsika komaso kudya midzimbe ndi anthu komapo amazitcha ku mdiopemphela kom pano zikut tangopitilizani kuuza anthu zanjira yakumwamba bs musapanga ziwiri zandalezi mudana.ndikholo lanu amene ali mulungu
Prophert mbewe abwera poyera mosaopa kuzuzula boma .kusiyana ndi achakwera anabisarila kuti Ndi abusa koma boza lokhalokha .oyitanidwa ndiambili koma osankhidwa ndiochepa .
Nankhumwa ndi wa mcp simuziwa
Continue 😂
Zoona zake
Very true
Sananeso MP wa DPP kut there opposition is doing nothing
Mawu amphamvu mr mbewe
It will be a very big mistake for people to vote for Nankumwa as a presidential candidate and he's not supposed even to be called Vice President of DPP. That's why DPP will have no future and it's shameful for the party that was strong to finish like that because of selfish people like this
Zoona kulibe oppositon kumalalawi kuma aphungu odzikonda ndi adyera osaganizira anthu osauka
Exactly
Thus my prophet talking ., Tell them.greedy zombies busy waiting for their turn to loot....sizitheka.
Things are not okay.... our country looks so pathetic
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Uĺaliki kuchokera palemba lanji m'baibulomo aneneri achinyengo ukatero naweso ukuzipangira kampeni
Ndinconco kumene
Kumeneko ndiye kuyankhura
Mulungu atisakhile president oopa mulungu
This is true
Za ziii.
Wat do u expect wen you put MSCE graduates to deal with crucial matters concerning the economy and country
Mfondo yabwino kwambiri a prophet
It's true though.
Zooona mbewe
Truth
Koma zokuti mudziko lamalawi zinthu zikusokonera chifukwa opposition leader ikufooka idzo ndiye zoona opposition iri mbali ya m c p osati anthu ndiye.kusogoloku adzitisokosa muvotere nankhumwa tidziti ndizolondola ?pomwe asakuyimira osauka .😂😂😂😂
Auzeni zoona Ali tondovi kupusa angoti ndwiiii kungoyanganira .
Chilungamo chimawawa, uyu chilungamo anabadwa nacho
Mawu bwana prophet
Zowona
Zowona zake,
Ndipo mulungu azikuonjezilani masiku ena amen
How can DPP oppose the government that the citizens chose to the best of their knowledge. The citizens said DPP was worse than mcp how then DPP can oppose what the citizens chose as best. Don't accuse DPP because of your wrong casting of your vote, don't push DPP to clean the mess you created on your own, be the solution to your political mess
Vuto atsogoleri anthu saganiza zokodza dziko lathu koma kutupisa mimba zawo
Ur prophet or multiparty member
Kaya ndi nneneri onyeli koma akunena chilungamo
Nankhumwa ndi mbuz
Ndipo ndikhazika ma speaker Ku parliament Kuti mwina nankhumwa amve
Kulidandaulila dziko
Zoonadi man of God
Sure farther tell opposite
Ndiwe cisilu ukunamizira mulungu eti
Mau zosaenda olo
Mneneli wonyenga uyu, mwa uyli mulibe umulungu
Kodi zome akunenazi ndi uneneri kapena zochitika
Zomwe akulankhulazi ndizonyenga? You must be very stupid citizen
Kkkk Anthu wenanu sidziwa kusiyanitsa zinthu.. apapa sakupanga uneneli apa akunena ZOMWE zikuchitika..kodi M kulakwa kudzudzula pomwe sipalibwino?? Huuuu umbulitu umenewu
Ndipo live this is true man of God
Munthu wamulungu sayenera kuopa apa ndiye waonesa kuti ndi mtumiki weniweni
Zoona
mawu koma awa Iwo Ali busy kunyoza chakwera chifukwa akufuna mpando zausatana basi
True
zoona
Well said fake prophet....
This time you nailed it.
Awuzeni busy kumangokangana uko
Nankhumwa empty head
Zoonadi dzikoli sililibwinoyi
dzidzudzuleni dzitsirudzi
Evil people what kind of man of God ?
Dude stay in your lane.
U clearly shows u know nothing about economy and procurement. Otherwise u should have talk of solutions.
Shut up neneli onyenga uyu
Wanyenga ndani
anthu panja amadana ndichilungamo
Pepani bwana, boza sitiliveka jekete ngati zikupweteka mukangoseka madata... Onyenga coz akunena chilungamo.
Mneneli onyenga ndi chakwerayo
Powerful
True