BON KALINDO -WANG'ALULA MCP,UTM NDI DPP LERO PA 13 August 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 сен 2024

Комментарии • 41

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 28 дней назад +2

    Now ndakhulupirilila kuti muthu uyu amayimadi pa chilungamo and sumaona chipani keep it up DC

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 28 дней назад +3

    Born kalindo the DC mumakwana mr

  • @MansonNyamwela-g5r
    @MansonNyamwela-g5r 28 дней назад

    DC, keep on kung'arula,lam following you live from dar es salaam, Tanzania...you are doing well job done

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 28 дней назад

    Kalindo Unstoppable, Untouchable Man the President of the poor Malawians ❤❤❤❤❤❤.

  • @WysonYassin
    @WysonYassin 28 дней назад +1

    Ndizodabwisa bwambili ame ikutilaandadi mangalimoto town zovesa chisoni ziko lathuli

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 28 дней назад

    Amene adalilodza dziko la Malawi adamwalira limodzi ndi John Chilembwe

  • @giftkamwiyo9175
    @giftkamwiyo9175 28 дней назад

    No fear for chikangawa

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 28 дней назад

    Malawi kuli president dziko la Malawi lakhala la manyi . keep it up freedom fighter

  • @JamesJohn-y5x
    @JamesJohn-y5x 28 дней назад

    The DC

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 28 дней назад

    chikangawa chikwapengesa mitu ndipo mituyawo szagwiranso ntchito ngati anthu mpaka choona chikangawa chitawoneka

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 28 дней назад

    The DC president wa anthu osawuka without you Malawi is nothing

  • @user-je8yo3zy3y
    @user-je8yo3zy3y 28 дней назад

    Pa graund pavuta koma Bon Kalindo Winiko
    Akusewela pompo ndikumawina kukadyela nyama ku Nyumba kwake ife kumapusa kuti akumenyela ufulu taiwala kuti ndi yemweyi anamunamiza kumupusisa Chilima kuti choka mu DPP.

  • @WandileTradding-ph6fb
    @WandileTradding-ph6fb 28 дней назад +1

    Musamanamize wanthu kuti mumapangila anthu osawuka

    • @JafaliChiwimbi
      @JafaliChiwimbi 28 дней назад

      Iwe kod akutuma

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 28 дней назад

      Ukuona kuti muthu wachilungano akunena zothandiza ngati zili zosakusangalasa ndi bwino osamavela chifukwa ifeyo athu ngati awa timawalemekeza

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 28 дней назад

    Amalawi Amasangala Munthu Nzawo Akamavutika, Mulungu Achotse Chiwanda Chaufiti Mwa Mmalawi aliyense, Kafukufu waonetsa kuti Mmalawi Aliyense Amatamba

  • @MapetoZwaneboy
    @MapetoZwaneboy 28 дней назад

    DC booorn kalindoooooo more fire 🎉🎉🎉🎉🎉

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 28 дней назад

    Mukaona munthu akutulusa ma vn daily dziwani kuti ameneyo mukumupangila ndalama ndiinuyo,

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 28 дней назад

    The D.C. woyeee ❤❤

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 28 дней назад

    Ku malawi kwachuluka achinyamata koma zili zisiru kwabasi munthu wanzeru zake sangamapope zopusazi

  • @CosterMustafa-m6h
    @CosterMustafa-m6h 28 дней назад

    Yomweyo boni kalindo 😅😅😅😅😅😅😅auzeni a amewo kkk akut mabhauza

  • @stanfordnsona
    @stanfordnsona 28 дней назад

    Kalindo ndizasangalala ukazakhala president

  • @ChristopherMunlo
    @ChristopherMunlo 28 дней назад

    Ndiwedi president weniweni, panopa kumozambic nyumba iliyonse akupeleka magesi aulele koma kuno mpaka zaka 4 ukudikira.bon kalindo ndiwe dolo umaionera patalli

  • @AustinBornface
    @AustinBornface 28 дней назад

    The DC!

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d 28 дней назад

    Chakwela sitizamuiwala ku mbili ino ya dziko lathu

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 28 дней назад

    Ndiopusa amenewo The DC

  • @EdwirnMatewele
    @EdwirnMatewele 28 дней назад

    Kodi uti chiyani sizikuveka wayiwala zolakhula eti magetsi ataniso kagwere uko iwe

  • @user-je8yo3zy3y
    @user-je8yo3zy3y 28 дней назад

    Lelo walasa ya magesi osati zina mmapanga zija.

  • @macleanldzimkambani7773
    @macleanldzimkambani7773 28 дней назад

    Koma achewa nda Lomwe simudzawamenyanitsa amenewa koma🤣🤣🤣

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 28 дней назад

    Pano ndikuwona kut bon kalindo zoyankhula zakusowa chifukwa zamagesi ukukambazo panopa ziliko bwino kusiyana ndi kale mages sachedwaso kukufikila kusiyana kale

    • @KhumboMunthali-jx5me
      @KhumboMunthali-jx5me 28 дней назад

      Wantopola iwe

    • @Edson-sj8vn
      @Edson-sj8vn 28 дней назад

      Mbali yako imeneyo ife six years yatha akungot wire ndi ma pole sizinabwere kod zimatheka kubweza ndalama?

  • @SamuBevulo
    @SamuBevulo 28 дней назад

    Mumayitha Mr DC

  • @HappyLester-c6j
    @HappyLester-c6j 28 дней назад

    Atukwan kwambiri DC

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 28 дней назад

    Mmalo mothetsa mavuto a Malawi they are busy searching for activists.

  • @johnarushamasese108
    @johnarushamasese108 28 дней назад

    ❤🔥

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 28 дней назад

    Zoodi DC mumakwana

  • @jameelmustaph8179
    @jameelmustaph8179 28 дней назад

    Inepano mages 3 years yodyesela mpaka 1milion koma mages osabwelabe

  • @jameelmustaph8179
    @jameelmustaph8179 28 дней назад

    Malawi mavuto okhaokhq😅

  • @lambaniedube9551
    @lambaniedube9551 28 дней назад

    Bornnnnnnnnnnnnn K..........,the ddddddddd cccccccc