Aukirana ku Unga. Chakwera atamudyesa nkhumba Sheikh ododoloka Ndalama

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 сен 2024

Комментарии • 52

  • @JosephLemani-qq1is
    @JosephLemani-qq1is 2 часа назад +4

    Asadzabwelelenso ku dpp komweko azidya nkhumbazo komanso ali moyo oipa kwambili osaganizila amalawi mmene likuyendela dzikoli ungajoine macp kuti amalawi azikuganizila bwanji

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 2 часа назад +4

    Komanso kuchisilaamu sitikumufuna 😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @GiftChilanga-u3c
    @GiftChilanga-u3c Час назад

    Sheikh Wadya nyama ya nkhumba ku UNGA tiye Nazo comrade ntanyiwa kkkkkkkk we proud with you

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d 2 часа назад +2

    Achita bwino kutengeka😅😅😅😅😅😅

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p Час назад

    Zoti analowa ku MCP analakwitsa koma zoti anadya nkhumba zabodyà chakudya chimene amadya ma president kumene apita tsanalengezepo

  • @GiftChilanga-u3c
    @GiftChilanga-u3c 55 минут назад

    Ntenje yemweyo amvekere iii n yama yanji yokoma ngati iyi sinadyepo ndipo wayamikira sheikh 😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁😁

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 2 часа назад +2

    Eeeeeee dyela .mix maluzi kkkkkkkkk

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 2 часа назад +1

    ANYANYA KUSUSUKAA.UNGA WOYEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEEE😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @GiftChilanga-u3c
      @GiftChilanga-u3c Час назад

      Woyeeeeeeee shehee yemweyooooo 😁😅😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @MustafaLikaomba-f3u
    @MustafaLikaomba-f3u Час назад

    Zilango zimenezo Za mulungu

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 2 часа назад +1

    A very good comment

  • @HakeemTepa
    @HakeemTepa 9 минут назад

    Akhungu okhaokha sangalolelane njila

  • @AdamuAsani
    @AdamuAsani 40 минут назад

    Ndikhumba kumene ameneyooo ntchitsiru 😂😂😂

  • @Muhamma.mdoloma.2001
    @Muhamma.mdoloma.2001 2 часа назад +1

    Haram !!!sheikh mtenje wapangilanjì😢

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa Час назад

    Kkkklkk pakana yakhumba. Wasala mutu wagaru kutengeka sanati

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 23 минуты назад

    Ndipotu waiyamikila akuchitakuti Yaku nonga' ndipo sungaidziwe imaoneka bwino kuposa inayo

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 32 минуты назад

    Apitiriza ngati wasanza

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 2 часа назад

    Kodi Mtenje wapita nawo? Mkuluyu ndi wadyera amuchita bwino pa msonkhano anachita kuzitamiliza kuti ndi Sheikh odziwika ku Mangochi.

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi 2 часа назад

    mwayenera kudya chotsikira dpp ndi chan inu mwakwera ya anthu osawaziwa kwao mwachita bho

  • @AmidyMudani
    @AmidyMudani Час назад

    Kkkkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂😂😂 samata kuwerenga ameneyo

  • @AlinafeChimoto-pp7wp
    @AlinafeChimoto-pp7wp 13 минут назад

    💪💪💪💪💪💪

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 42 минуты назад

    Kkkkkkkkk kususuka,,azikhala konko

  • @DaudiLesta
    @DaudiLesta Час назад

    Akabwera amphedwe wa dyera ameney

  • @HenockKabuya-v1k
    @HenockKabuya-v1k Час назад

    Anthu akutengeka NDI zaziii

  • @isaacbandah3617
    @isaacbandah3617 Час назад

    Kkkkkkkkkk yomweyo mtenje iweeeee 😂😂😂😂

  • @user-iz1qi3db2g
    @user-iz1qi3db2g 3 минуты назад

    Wow 😂😂😂

  • @BittonRashid
    @BittonRashid Час назад

    Zausilu kwabasi unthila kuwili

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala Час назад

    Amuchita bwino kususuka

  • @GiftGiftmanison
    @GiftGiftmanison 33 минуты назад

    Ndchisilu amuchita bwino

  • @ChibakuliKaisi-cm3hn
    @ChibakuliKaisi-cm3hn 2 минуты назад

    Atenje khuyalukha 😂😂😂alithongo

  • @GiftWilliam-t1z
    @GiftWilliam-t1z 25 минут назад

    Kkkkk watiojeza kkkkk koma ku Unga yavuta.

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 часа назад +1

    Kufuna ponyozelapo Asilamu apa zikugwilizana bwanji wayipa chifukwa walowa mcp adali wabwino ali ku Dpp kodi mtenjetu ndi ozindikira pa chipembezo okay musalowese ndale

    • @chilembwekanjirawaya4296
      @chilembwekanjirawaya4296 2 часа назад

      Akukamba za nkhumba osati ndale ayi wayamba misala

    • @BairdThomas-c2k
      @BairdThomas-c2k Час назад

      vuto ndiloti iweso bekon sukuiziwa ukuona ngati akupanga ndale nanga ham iwe ukuiziwa

  • @mickyhassan3178
    @mickyhassan3178 2 часа назад

    Timuthira

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb 2 часа назад

    Adya liguluwe kkkkkkk amwalimu

  • @GobaBarton
    @GobaBarton Час назад

    Kususuka

  • @AkibuMdala-sr1dy
    @AkibuMdala-sr1dy 2 часа назад

    Komaso bora akanamudwesya ya muthu😂😂😂

  • @EmmanuelMpalagule
    @EmmanuelMpalagule Час назад

    Kkkkkk amudyetsa liguluwe mmmmmh mcp msambi kkkkkk

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 2 часа назад +1

    HARAM!!!!!!!!

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel Час назад

    Dyela..sheikh wakuri?

  • @DavidMbewe-r1f
    @DavidMbewe-r1f Час назад

    Ntenje iweeeeeee🤣🤣🤣🤣

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 4 минуты назад

    Kkkkkkk chilango chilipadziko lapansi pano

  • @ShillaShamil-v2y
    @ShillaShamil-v2y 59 минут назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x Час назад

    😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😮😮😮😮

  • @LoydKamtedza
    @LoydKamtedza 59 минут назад

    Ife ma Muslim sitikufunaso 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 okudya nkhumbao walowa kale Christ okumwa magazi asataniki. Mtenje uzidya nyama za anthu ndiwe galu wDyera

  • @HalimaKaisi-w7j
    @HalimaKaisi-w7j 44 минуты назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @PatrickTembo-zn6vy
    @PatrickTembo-zn6vy Час назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @BairdThomas-c2k
    @BairdThomas-c2k Час назад

    kkkkkkk