Say No To Age Limit - Comrade Ntanyiwa
HTML-код
- Опубликовано: 5 сен 2024
- Today on Nyasa VoiceBox we feature Comrade Ntanyiwa who speaks on the issues of age limit being proposed in Parliament and upcoming demonstrations by Malawi First Movement.
Lero pa Nyasa VoiceBox tikukupatsirani Comrade Ntanyiwa yemwe amakamba nkhani zokhuza zaka zomwe zikuyenela kuperekedwa ku Nyumba ya Malamulo ndi ziwonetsero zomwe zichitike ndi Malawi First Movement.
#malawi
Apm my vote 🗳
Sitikumufuna nankhomwa
Malamulo samasinthidwa pofuna kumulepheretsa munthu m"modzi amenewo ndi maganizo opusa
Ntanyiwa is my boss
Athanyiwa zikomo kwambili pomenyela nkhondo anabanda kuthekerani anamalunga kuchikwawa anyajere kuzimba anagozo kumwaza abiti issa mangochi ndi Mandela ose mmalawi ambuye apitilize kukudalisani anyamatanu pa izi mukuchiti amalawi ovutika musaleme may God blessed you all guys
If we go ku mademo in numbers with serious faces, that foolish bill will never pass
Nankhumwa misonzi a amalawi ovutika Ife ikangotsika,dziwa Kuti mulungu achitanawe ndipo zosatila zake ndi tembelelo looopyha kwambiri
Nankhumwa must be very careful with Malawians and never take them for granted.
Let's go guys ife kuthyolo tili okonzeka kuma damo nankhumwa sitikumulola olo adad oyeeeeeeeee
ApM my vote
Iwe panyapako tipanga mademo ngakhale satipindulila komano sitikufuna malamulo awanthu muno ongopanga chifukwa anadana
Nankhumwa panyelopako wava,ndikila tisinthe dzina lakolo aise
Ndipo ndi garudi weniweni
Musaiwaletu paja ndi Chi Robot"Chakwela."
All members talking about this bill are fullish
Age limit zofoyira, malawi kadziko kakangono kosauka kodalira kupempha ku mayiko omwe zikulamulira ndi nkhalambazo mayiko awo mkumayenda bwino kodi anankhumwa mukupengatu inu ,ndipo apapa mwatha ikhala mbiri chabe no age bill in malawi zopusa zakozo ife ayi mzeru ulibe.
Malawi constitution must be protected and no way can any law in it, can change just because of MCP. MCP party, should not forget, Malawians voted for referendum because of shits which they were doing for 31 years.
Tiyambe tapita kaye kunyumba ya Nankhumwa tikaiotche.
From there to parliament tikaiotcheso , ndipo palibe angafuse cause ndindalama zathu.
Za ege zimenezo zawonekelatu kuti ndi nsanje ya anthu pa ena ndiye zonkhudza malamulo zimanwela kaline vuto izi zabwela palivuto loti anankhwa achotsedwa muchipani sizonveka takana
Nankhumwa zamuvuta ziko lamukana athera ku mcp amasusa chipan chake chomwe
Kod namkumwa ali ndizaka zingati? Thandizeni amzanga? Zikuonesa ngat ali ndi zaka 14
Amalawi tatopa and kutopa kwathu adakutenge ngat kupusa
Tiyeni kumadem komwek kupalamet ad this tym palimbe azamangidwe loya wakhul gat ine ndizakala nanu komwek
Ndipotu kupanda ntchito kwamunthu wachikulire oyamba kuwona akanankhala mulungu koma mulungu pofuna kugwilitsa ntchito munthu amasankha ukwima zalu kumene ndipo anthu atalankhula momaliza pabanja la ablaham mulungu anabwelersa chodwabwitsa pabanjalo nawapatsa mphatso ya mwana muukalamba mwawo tsono kukula tisazintege gatikuti mulungu amankha kuti wachokapo ayi munthuyo amankhalabe akugwilabe ntchito ndi mulungu ndipo mulungu yo ufumuwake umakulane mwamunthuyo izi tikupaga amalawi tikupitilizabe kukuza ukali wa mulungu chifukwa mulungu pamunthu aliyese mwiniyen yenkha amadziva ulemelero izi tikupalamura kachikena tinapalamula kale potenga ntimiki wake chakwsla kumuyika mulamulilo wadziko lero mulungu dziko walinyanyala apa tikulimbanaso ndikukula kwa munthu kudi amalawi tilipakati polimbana ndi mulungu ndinthu?
No ege limit
Zavuta iyi mathelo athawi
Ali kuno timamuona ife Ben longwe sanapite ku malawi ,.. ndi mwana opoira
APM woyeeeeee
Nankhumwa amakonda ndalama ,alibenso ndi fundo zomwe
Chitsilu iwe mntanyiwa
Age limit taikana sitingamve zimenezi and Leader of opposition akhale amene asankhidwa panoyu Not theirs
Apm yomweyo
Amalawi sitilola manyi age limit
Nfundo zaanthu ofunira dziko lawo zantendere osati ben longwe chimunthu chaulesi
Chipani chamagazi chikufuna kuphesa amalawi .chifukwa amalawi 1 party sitingairole ndipamene pazaoneke magazi
Born karindo malawi first tiyen tiyen pamsewu
Inu nonse Mr Mtanyiwa ndi anzanu onse komaso ndi chanel iyi ife timakunyadilani kwambiri.And inu mukuyenela kudzathokozedwa mokwana adadi akatenga boma.Mikigwila ntchito yotamandika kwa mtundu wonse wa Malawi.Mukadzapatsidwa mwayi tikalowa m'boma pls osadzalola adadi kulandilaso anthu osagwila ntchito anthu omangodyela mundalewa ayi.
Komanso amalawi tasowa utsogoleli obweletsa mfundo zotsutsaboma zoyenela mpaka zaka 4 lelo atibweletsele za ege ai sitikufuna zimenezo
Aaaaaaa anzanga pitanidi pa msewu nankhumwayo ndimbuzi. Anthuwa akufuna kuyambutsa nkhondo ndiye chonde chonde osavomeleza. Tiyeni tinde or kukafika pa nyumba pake. Aaaaaaaa ndayikonda ifeyo tikufuna pitayo ndi iyeyo alindi chani?
Tili pambuyo pani
Kondwani Nankhumwa machende ako usakakamire udindo anakuchosa Ku DPP pano ndiwe Munthu wamba machende ako
Kutengela momwe boma lilipoli linachitila mosogozedwa ndi antambo achilima achakwela mademo ndi othandiza moti panopa amalawi tigwilanemanja ndi antanyiwa ndi the dc kalindo tipambana
Kapanda mchokelo anakodzela moto wa ana
Ben Longwe wabwerako ku joni ataonda Edzi yamukwapula anthu Mukuyesa njala, mankhwala akumwawo wayamba kusapota mcp yet amamunyoza chakwera, ine ndi wa MCP Ben Longwe asabwere kuchipani chathu yayi
No
Timugwirizana nazo zimene anena a Mtanyiwa 100 perecent we Malawians we dont want age limit bill ni vindere vanakondwani Na khumwa stupid foseki age limit iyambire pa A P M ? Likalekelachi kuyambira paKamuzu Banda 93years kiimila MCP
Nankhumwa please don't take malawians as fool ,one day u will regret.😮
Nakhumwawangoononga c v yako palibe yemwe angamukonde amtanyiwa ndi zoona zomwe mukukamba munthu wanzeru sagalowe.ku m c p mmene cakwera akudzunzira anthu ndiye udzikati ladzalo mmmm
Nankhumwa is fack
Timugwirizana nazo zimene anena a Mtanyiwa 100 perecent we Malawians we dont want age limit bill ni vindere vanakondwani Na khumwa stupid foseki age limit iyambire pa A P M ? Likalekelachi kuyambira paKamuzu Banda 93years kiimila MCP