ZIFUKWA ZOMWE ZINAPANGITSA BANGWE SDA NDI MA CHALICHI 10 AKU ZAMBIA KUTI ATSEKEDWE.

Поделиться
HTML-код

Комментарии • 80

  • @TiyamikeMollen-m4r
    @TiyamikeMollen-m4r 6 дней назад +5

    BUT THIS THING OF MAJORITY LEAD! EESHEE , MAY GOD HELP US AND WE NEED TO REMEMBER OUR GOD DOESN'T USE MAJORITY.

  • @frankjamesmanere9470
    @frankjamesmanere9470 4 дня назад +2

    After realizing that there is nothing but pure politics in all churches and considering myself non partisan, I just stopped being a member of any church

  • @WandaMinjale
    @WandaMinjale 7 дней назад +5

    Mukhonza kutseka church koma simungawatsekere kumwamba mpingo wa seventh-day lero ndi dimba la akulu akulu akumipando

  • @marykaneka6878
    @marykaneka6878 7 дней назад +3

    SDA inali kale zakudya za lasabata tikuphikilatu friday.

  • @CeciliaMakina-z3s
    @CeciliaMakina-z3s 4 часа назад

    Ngati mukinamizana kuti mulanda mslo sizithrka Mulungu sliko ndipo wavomera Bangwe ngati church pachokha mukupanga zinthu kuimunthu osati zauzimu ayi Bangwe wagwira choonadi.

  • @nahawasteven6051
    @nahawasteven6051 День назад

    A Bangwe ndikukulimbikitsani kuti chomwe mukuchita ndi cholondola .Anthu awa omwe atseka mpingowu ndiomwe amphatikana ndi mafano ndi president wao.
    Mosatila Bible chachikhumi sichiyenela kupita ku office (conference) chikuyenera chikhale panpingo ( Malaki 3: 7-8 komanso 1timoteyo 3:15 .)
    Chomwe akuchita anthu awa ndi dyera si chi khristu-yi.
    Mulungu awakhululukire.

  • @RobertMaganga-w8d
    @RobertMaganga-w8d 3 дня назад

    If indeed some issues have been tramped against them its unfortunate remember how Jesus was crucified by elders .Are the acts out of 28 Fundamental beliefs? I pray God intervene inwardly so that Bangwe is saved with the guidance of Holy spirit.

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 7 дней назад +2

    M'busa oyipa iwe Bangwe SDA ikutsata zakumwamba

  • @HarlodHarneck
    @HarlodHarneck 7 дней назад +2

    Who give you this power to close the church of God....mukusiyana pati ndi afarisi achinyengo akalero

  • @AllanMwakalenga-wn5ib
    @AllanMwakalenga-wn5ib 7 дней назад +4

    Kupewa maphokoso Chinyumbacho asiyireni,mangani china penapake

  • @BenjiMtonga-n8b
    @BenjiMtonga-n8b 7 дней назад +2

    Koma abale anga kunali bwanji bangwe SDA mukanayisiya kusiyana nsikutseka

  • @owenmanda8521
    @owenmanda8521 4 дня назад

    Ever since I was born l used to see the Three Angels Message sign from nowhere l just started seeing this new sign with the cross facing downwards some changes developed even the women ministries uniform from Blue and White and now maroon and white was implemented l don't know why but something fishy must happen from the to offices of the church.

  • @BilliatEvance-kr1mh
    @BilliatEvance-kr1mh 2 дня назад

    How do you know kuti a Bangwe akulakwitsa? Ngati a Bangwe akulakwitsa simukuona kuti oyamba ndinu before abangwewo chifukwa mumkatsatira zimene abangwe akutsatira pano? Ngati a Bangwe akulakwa chifukwa chotsata dongosolo la kare, kalero imene inali SDA, simukuona kuti bangweyo nde SDA pamene inuyo mwayamba zatsopanonu nde Mpingo owukira chifukwa simukutsata maziko ampingo wakare?

  • @JosephNjala-c7u
    @JosephNjala-c7u 7 дней назад +1

    Signs of the times. Bangwe SDA sikunana i support but pokana Holy Spirit mmmm

  • @chrissyamanda5510
    @chrissyamanda5510 7 дней назад +2

    Ndiye Logo mudayisinthilanji pomwe 3 angels ndi Logo ya kalekale mu SDA?komatu ku union kwanuko ndinu olephela kwambiri
    Mpake TY Nyirenda ali busý ndi zandale
    I support bangwe
    Ndalamazo nzawo osati zanu
    Vuto mumatenga ndalama zonse kusiya mpingo ulibe chilichonse
    Aaaa zafikapa ambilife tisiya kupemphera
    Ndinu anthu oyipa
    Ndipo SDA yalero sikudziwika komwe ikupita ndi zomwe ikuchita

  • @georgechikafutwa1334
    @georgechikafutwa1334 4 часа назад

    Ine nkhaniyi imandimvetsa chisoni ndikamaimva. Kodi ngati mpingo mwayesa kuupempherera mpingowu like kusala kudya ndikupemphera? Why tokhatokha pansi pano kusalana?

  • @blessingsdangwerobert6432
    @blessingsdangwerobert6432 6 дней назад +1

    Asatinamize awa , nkhani yeni yeni imene atsekera Bangwe SDA ndi chachikhumi. ofcourse azimai akuyenera kutumikira not like in pastoral and elders office. This is unwise decision mutha nazo nazo mipingo izi. Inunso mukuyenera musamadye tithe because mumakana kusunga sabata molingana ndi Bible, komanso uthenga wathanzi, mukulimbikisa make up mu church!! tikuyenera kutseka ma conference... 2) kodi conference ndi nyumba yosungiramo tithe imene Mulungu adanena? Onyenga inu! ana anjoka!!

  • @Rebecca-n6b4h
    @Rebecca-n6b4h 13 часов назад

    Inuyo ndinu okhumudwitsa bwanji munasiya sign ya Angelo atatu aaaa sda inali kale mwalowa chikunja

  • @HealyNamowa
    @HealyNamowa 6 дней назад +1

    Tingo khala ndima confaresi awiri yatanda ndiya angelo atatu

  • @WysonKhaweke-v4g
    @WysonKhaweke-v4g День назад

    Abale ndi alongo a Bangwe SDA Church,limbikani kupemphera chifukwa Mulungu, yemwe sasintha komanso samalola kuphatikizidwa ndi nyasi, ali nako kuthekera kobwezera SDA Church pa dziko lonse lapansili ku mayendedwe ake akale. Abusawa ndi anthu ndipo anthu ndi okhumudwitsa kumene nthawi zina. Ndikati "Bible!" Mundivomere mwamphamvu kuti "Bible lokha basi!"

  • @InnocentChinkhosa-l3j
    @InnocentChinkhosa-l3j 8 дней назад +2

    Manual imaletsa mpingo kukhalandi maloya komaso khani za mpingo kumapita khothi la dziko.lapasi pa ziphuzitso za mpingo.

  • @ThomasMangilani-d9j
    @ThomasMangilani-d9j 8 дней назад +2

    Mukutikila Ndani mulungu kapena munthu ngati mutumikila mulungu asiyeni oweruza ndimwini

  • @PaulManyamba
    @PaulManyamba 7 дней назад +2

    Mwaseka ku thipi koma kwamulungu ulipo mpingo

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 7 дней назад +3

    Cash is the problem turned into business

  • @MAsd-r8s
    @MAsd-r8s 8 дней назад +3

    Zimenezo zamveka, koma ine sindikumvesa pa log yathu inali ya three Engel's , tsono chizindikiro cha lawi lamoto ndi ntanda chabwera bwanji?

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc 8 дней назад +1

      Log imeneyi ya moto ndi mtanda ndi log ya catholic.titha,kusokonedzedwa,ndi azitsogoleli.kuyambila,kalelo mpingo wa mulungu susitha bwanji, lero akufuna ku sitha and,tikamawelenga, bible limati kazi akhale wachete

    • @chrissyamanda5510
      @chrissyamanda5510 7 дней назад

      Mposo
      Akutipstsa mtanda ngati timagwilitsa ntçhito mtanda
      Kutipatsa chi logo cha catholic
      Anthu oyipa awa

  • @tinkaphethi1395
    @tinkaphethi1395 6 дней назад +1

    If I understanding the president for SDA, he has vehemently said, anything that applies to SDA must be based on the teaching of the Bible...I would have loved if such verses would have been brought up for the attendants to have them.
    1. Which verses do allow any Christian church to allow women to usurp authority over men
    2. Which verses say, there is trinity
    I think beside their accepting and denying the church logos...the preceeding are the main bone of contention.
    I think the main issue here is: majority of Adventists are preferring changes to suite modernisation. You will agree with me that even when questions or contributions were accepted, someone recommended for gender balanced coverage. I guess the teachings of SDA are changing gradually because of the ministers who tap some changes that are adopted from where this denomination came from. America....
    The best would have been prayer and Word( Bible)...I think this would have resolved this problem...

  • @binalidjeyshabahzombamalawi
    @binalidjeyshabahzombamalawi 6 дней назад +1

    Tilindichiphunzitso chimodzi ngat akupanga zosemphana ndi real SDA oukirawo achotsedwe.. Remember mu the Holly Bible muli Esther ndi maina ena aakazi zomwe zikutanthauza palibe cifukwa cowasalira azimayi..

  • @chifundochibalaka8439
    @chifundochibalaka8439 День назад

    SDA ndikuidza ine singapange izizi apapa mpingo otsala uja watsala kupita kumwamba ndithu chifukwa izizi sizoona koma mkatolika uja mmmmmmmmm mpaka kugwedeza mpingo chonchi apa wabalalitsa nkhosa koma mulungu Ali ndi anthu ake kaya tikasonkhana kutchire palibe vuto bola ambuye kukhala nafe

  • @JaneChipolopolo
    @JaneChipolopolo 8 дней назад +4

    Ephraim waphatikana ndi mafano angel atatu mukukaniranji

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 7 дней назад +1

    Ngati mukulephera kumvesesa kuti pomwe pagona nkhani ndi posintha ziphunzitso za sda ( chinavuta nchiyani ndi three angels log?, nanga mukunena zosiyana ndi poul chifukwa chani)

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 7 дней назад +1

    Nonse mukulengeza izi ndinu ziwanda samalani khalidwe lofuna ndalama mulangidwa

  • @OskarJela
    @OskarJela 8 дней назад +1

    Amen

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 7 дней назад +2

    Mbusa wachinyengo iwe wachikangawa iwe mesa wadya ndalama zamagazi iwe

  • @charitymhone9983
    @charitymhone9983 6 дней назад

    Nanga log mwabweretsa yo ikuthandauza chani la malawi amoto ndi mtanda, kusiya ya Angelo atatu.ndpo anakana kt mzimayi azikhala mbusa not kulalikira..wagwa babulo ndpo akukukwakwazani simunati, nanga chomwe mlesela ndi asalalike za Buku la chibvumbulutso ndi chani, ana anjoka inu kumapanga za ndale ndi chikangawa mbali ina za church chokani takudziwani pano mkhaula

  • @VincentHussein-r9n
    @VincentHussein-r9n 9 часов назад

    Mulungu wakumwamba amene amaziwa zonse azaweruza yekha

  • @MelitaFrancisco-g7u
    @MelitaFrancisco-g7u 7 дней назад +1

    Muziphuzitsa zifukwa zomwe kale kale timkagwiritsa ntchito logo ya angelo atatu
    Chifukwa chomwe kale azimayi samalalikira mkachisi
    Then explain the meaning of New Logo
    The reason why now women are allowed to preach
    Zikhoza kuthandiza
    Even myself I don't know the meaning of the Logo ya sda even though l am one of sda

  • @WinnieMtelekesya
    @WinnieMtelekesya 7 дней назад +1

    This is really sad,God help us

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 7 дней назад +1

    Mmmmm boza inu mukambayo nkhani ndiyoti amakana kupitisa ndalama ku field yanu

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 7 дней назад +1

    Munasokoneza mpingo atsogoleri adyera komanso achinyengo

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 6 дней назад +1

    Amene adabadwira mu SDA church avomereze kusekedwa olo kuno Ku south Africa SDA churches sakuphizisa zomwe ife timadziwa ngat saziwa kuli bwino asiire azawo odziwa

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h 7 дней назад +1

    Ndichifukwa ine ndinasiya kupit mmachalichi alawi ya moto bs mtanda

  • @BensonFinigile-h5f
    @BensonFinigile-h5f 7 дней назад +1

    Benefits mumapeza chachikhumi chimapita kuti inu

  • @AlexanderKaunda-mc6vv
    @AlexanderKaunda-mc6vv 6 дней назад +1

    mulungu atithandize kwambili

  • @BenjiMtonga-n8b
    @BenjiMtonga-n8b День назад

    Koma zimene mukupanga mu mpingo wathu muzawotchesa anthu ambiri, and what should you know is God does not choose people but majority no this thing's what you did 😢😢 I'm feeling sorry,if you can look the first person from five you choose if you could listen to that one😢😢 you could have a better good ideas but that person you cut his message and you reject the truth and there is no true in you pastors

  • @chimwemwegomani3359
    @chimwemwegomani3359 7 дней назад +1

    Vuto azibusa athu akulandila salary and akuti malamulo.a mpingo osati bible

  • @YamieTiyesi
    @YamieTiyesi 7 дней назад +1

    Tsekani church anthu oipa akubangwe

    • @gracioussinoya2850
      @gracioussinoya2850 7 дней назад +1

      Palibe zimenezo aise ineyo ndiwakundirande ndipo ndine wa mumpesa wanyooo bangwe sda sakulakwa chotsekera church mchiyani?

  • @VanPaul-sv9yx
    @VanPaul-sv9yx 7 дней назад +1

    Ngakhaleso kumwamba kukupita anthu owelengeka

  • @GiftSoko-w4h
    @GiftSoko-w4h 7 дней назад +1

    Matsiku osiliza mupaka kuseka church 😂😂😂😂koma ziko ili

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 7 дней назад +1

    Koma anthu inu ndye mukunyozana ngt siinu a modz mwanji

  • @Alomwe
    @Alomwe 4 дня назад

    Nkhani ndi ya ndalama zinazo ndi zaboza

  • @Bakire-y1o
    @Bakire-y1o 7 дней назад +1

    End times, dyera bas.

  • @VanPaul-sv9yx
    @VanPaul-sv9yx 7 дней назад

    Mpingo wa Seventh day pano unataya direction, ndiizi zalowa ku nthupi apa mzimu wa Mulungu palibe

  • @BensonFinigile-h5f
    @BensonFinigile-h5f 7 дней назад

    Chokani inu ana opanduka mukuchita zadzko osati zakumba khalani ndi chi church chanucho

  • @nahawasteven6051
    @nahawasteven6051 День назад

    May God forgive you for you know not what your doing, you can't close Bangwe as if you Are God.

  • @InnocentChinkhosa-l3j
    @InnocentChinkhosa-l3j 8 дней назад +1

    Avoid makhothi .adziko lapasi pankhani za mpingo.maka pa ziphuzitso.

  • @PitsonKamuyango
    @PitsonKamuyango 8 дней назад +2

    Bangwe SDA church is not to blame

  • @BilliatEvance-kr1mh
    @BilliatEvance-kr1mh 2 дня назад

    What made you to remove 3 Angels, should we say you wrong church the time you were using 3 Angels? Where is the verse which allows women to preach?

  • @fae6833
    @fae6833 7 дней назад +1

    Kampingo kozikonda aka. no wonder failing to resolve a petty issue. Go back to how this church was found you will understand why the current confusion.

  • @NickeshNdagama
    @NickeshNdagama 6 дней назад

    indeed we're near end time

  • @edsonndalama2334
    @edsonndalama2334 8 дней назад +1

    Logo ya angelo atatu yo mukuipezera kuipa pati? And anaibweretsa koyambako ndi ndani? Mikangano mmipingo ngati zipani za ndale

  • @BensonFinigile-h5f
    @BensonFinigile-h5f 7 дней назад

    Mbusa wachinyengo uyu panga inu ndo chi conference chanucho ife tikupita kumwamba

  • @givennyirenda112
    @givennyirenda112 7 дней назад

    Apule nanu mwalora church ku tseka??

  • @stormchatepa134
    @stormchatepa134 7 дней назад

    Zazi

  • @BenjiMtonga-n8b
    @BenjiMtonga-n8b День назад

    Your the one you refuse the truth because you rejected the three angles logo and the three angles message, your just the same like Diop and the GC READERS FROM AMERICA

    • @BenjiMtonga-n8b
      @BenjiMtonga-n8b День назад

      there is no truth in you brothers, and what you did some like Judas Iscariot😢😢😢

  • @felistasbunu9824
    @felistasbunu9824 7 дней назад +1

    1:09

  • @givennyirenda112
    @givennyirenda112 7 дней назад

    Kodi bangwe SDA akulalikira zaufumu wamulungu kapena ayi?

  • @JohnKachali-ud2ll
    @JohnKachali-ud2ll 5 дней назад

    Amen

  • @felistasbunu9824
    @felistasbunu9824 7 дней назад +1

    4:33

  • @givennyirenda112
    @givennyirenda112 7 дней назад

    Apule nanu mwalora church ku tseka??