Tinyimbo tofewa, kupereka uthenga wa chiyembekezo chabwino ku dziko lathu la Malawi pamene anthu akudutsa munyengo zowawa kwambiri pa ulamuliro wa Chakwera. Mulungu atithandize ndithu
The best political song ever in my view. Atolankhani amabungwe amipingo ndi azipani kodi mukudziwa kuti nditapita ku NRB ndapeza National ID yanga akuti was issued pomwe ini sindinapatsidwe? Kodi ziphasozi zikumapita kuti? Motero pakanali pano sindine wokhutitsidwa kuti chaunzika chidzagwiritsidwe ntchito povota. Lamuloli likufunika likasinthidwe mwachangu ku Parliament.
Osamasewera ndi azimai awa❤❤❤❤
Hit of the year !!! 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💙💙moto unandiiiiiii
DPP iri ndima shick osambat osati ajessey kabwila arimbu khope ngat amachenjra kumwa ambuyentenga
😂😂😂 ambuye m,tengeni ambuye m,tengeni hiaa
Upole moto
Ine ndimwana wa adadi and nzakhala mwana wawo forever dpp my favorite vote 💙💙💙💙💙💙♥️
More fire azimayi nice song ❤❤❤❤❤🎉
Gud one,,APM DPP my vote
Tinyimbo tofewa, kupereka uthenga wa chiyembekezo chabwino ku dziko lathu la Malawi pamene anthu akudutsa munyengo zowawa kwambiri pa ulamuliro wa Chakwera.
Mulungu atithandize ndithu
This song eish bravoooooooo
This is amazing song and 2025 bomaaaaaaaaaaaaaa 🎉🎉🎉🎉🎉
The song of the year❤❤❤
Azimayi awa 🙌🙌🙌🙌
The best political song ever in my view. Atolankhani amabungwe amipingo ndi azipani kodi mukudziwa kuti nditapita ku NRB ndapeza National ID yanga akuti was issued pomwe ini sindinapatsidwe? Kodi ziphasozi zikumapita kuti? Motero pakanali pano sindine wokhutitsidwa kuti chaunzika chidzagwiritsidwe ntchito povota. Lamuloli likufunika likasinthidwe mwachangu ku Parliament.
Azibusa sitimamvina koma nyimbo zaazimai awa azibusa ambiri timamvana basi😂😂😂😂😂
Colour ndi yomweyi💙
Pain Goes straight kwa Danlu
The composers are super
Azimayi awa amaswa Sound yabwino kwambiri
Boma ilo 🎉🎉
Sindikuziwa ngati kutazapezekeso chipani chokoma ngati ichi
🎉🎉🎉 ina ijaso ya chiyawo ija plz❤
😂😂😂😂😂Koma kwakomatu
❤❤❤❤❤ more 🔥 my vote
Iyi yamubaya wa Chikangawa 🔥🔥🔥🔥
Wazimayi wakwimba awa eee
Kumangokamba nkhani sikupindula koposa mawa achotsedwe bas
Zilibwino kwambili❤
Boma ilooooo 🎉🎉
Azimai akuimba awa ❤️❤️❤️❤️❤️❤️🙏❤️
N,sokhano waathu ovesesana🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤
Peter ndi lawyer kale. Komabe uthenga wamveka.
Beautiful song🎉🎉🎉
Azimai obhebha ❤❤❤
a Dpp. Timakudalilani kma tapangani chani. Galu uyu chikangawayu. akufuna nkhondo. Tamuchotsani. Mawali ma demo pls pls. Tawauzaniso a dad wo
My vote
That's the best track DPP 2025 boma
More fair azimayi
Zilibwino❤❤
Nyimbo iyi injenjemelesadi aChikangawa. DPP moto!
Nice song .....DPP WOYEEE
Love it
Mwadza inuyo
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
My Vote❤❤ DPP
Truly game chenger atupele ali mmadzi adad apeleka ufumuno kumpoto
Even a opposite amalaka laka atawapanga hire🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Boma mwatenga kale
Zilibwino 🎉🎉🎉🎉
Dpp niakatundu🥰🥰
Sure ❤❤❤❤❤❤❤💃💃💃💃
Nice song
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Moto adadi
❤❤Beautiful
Mbambande
koma azimayi asendeza a dpp amadziwa kupeka nyimbo mmm
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
❤❤❤❤
Using ladies but beautiful song osat ma millions kma mbola 😂
nyimbo yoti utha kuika pa reapet
🎉🎉🎉🎉
Zabwino ndithu
2025 boma❤️♥️
Exsodo 14:13:14 siku lina titulukamo moto
The song of the year❤❤❤
My vote
❤❤❤❤❤
🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤