Sizingatheke kumugwira dilo wanga history is the best teacher osaopa ndizipemphera kuti titeteze history is the best teacher bakili muluzi TV you are the best one palibeso wina angafike pa iweyo ndiwe otetezeka ndi mulingu
Machine emenewo akanakhal kuti alipo bwezi kwa America kulib umbamva ndi umbanda komas dziwani Mulungu amuteteza Bakili Muluzi TV ndpo adzafa kufuna kwa Mulungu pliz nthawi yatha iyi America akanakhal chisanzo koma ai machimo kumangochitabe shame
Akunana padziko lapansi palibe matchini otelewa akungofuna kutibela misonkho yathu asatipusise komanso olo atachigula asadzinamize kuti angamupeze ntanyiwa ndi Bm tv anyamata amenewa amayidziwa kopyuta koopya ku mcp kulibe. Bm tv ndi ntanyiwa ndiomwe amatiuza zoona osati mbc ndipo ndiyomwe timavela history iz a best teacher
Boma likulephera kupereka ndalama kwa a Malawi omwe anapuma ntchito Zaka ziwiri ena zitatu zapitazo koma akufuna kugula Makina kugwirira anthu what a shame
Ayamba kugwidwa ndi omweyo abomao koma Bakili Muluzi TV Mtanyiwa ndi akatundu mitunda ya phiri la Mulanje panchombo peni peni pa phiri lalitali la Mulanje zizivutani kuleka kuti mugule fetereza anthu anthire mminda mwao panopo chimanga chayamba Madera ena kumasula chopanda fetereza zopepera basi dziko la umasikini ngati linoli
Pamenepo ndipamene mziwe kuti mnasankha manyaka a presdent and his full squad cz malo mopanga zinthu zoti ziko lipedze mafuta komanso fertiliser ndi so njara yeti kumakhala busy ndi anthu omwe a kuwauza amalawi chilungamo zopusazi koma
Koma mitu yanu ikugwira? Mmalo mogula Mafuta Anthu ma business ayima kusowa kwa Mafuta, Njala ili mbweeeee. Boma lauchitsiru. Akufuna kupakula CHAKWERA 😂😂😂😂 Koma yaaaaaaa MALAWI wanga
Sizingatheke kumugwira dilo wanga history is the best teacher osaopa ndizipemphera kuti titeteze history is the best teacher bakili muluzi TV you are the best one palibeso wina angafike pa iweyo ndiwe otetezeka ndi mulingu
Koma ndalama ikuyabwa ndithu , kusiya kugula mankhwala mzipatala anthu akufal , mwinadi angofuna mobela ndalamayo , mmm history is the best teacher
Kupanda bakili muluzi TV bwezi tili muumbuli waukulu example zomwe a MCP ankapanga mbiyomu komaso pano
Bakili muluzi...ndi deal ...simuwapeza....onse history...is the best Teacher.....mukunama....Anyapapi inu
Chipani Cha MCP anthu ake ofoyira mithu
History is the best teacher ✅✍️📺📻📖📪📖📚
Bakili muluzi tv is better than zodiac
Ife timakonda kumva chilungamo from bakili muluzi tv
Akuzinamiza kwambiri Bakili TV Forever ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
History is the best teacher
😮akufuna kungwilisila pozabela kubela mavote chifukwa smartmatic agonjesendwa
God he will protect bakili muluzi TV MACRA and chakwera machendanu
Sangamupeze amene aja ndi akamuna, our Living GOD is going to protect him
And more over anthuwo they talk truth
Chakwera alibedi zelu zoodana kudana ndichulungamo ukunama koma simuwepezabe history is the best teacher
Kkkkkkk Koma ndaseka
Clif chinyama ntanyiwa the dc Bakili Muluzi 📺tv anabwera basi history is the best teacher
Ifé tikufuna mutipatse fertilizer tigule pamtengo ozizila
Ngati ali abodza bwanji mukulimbana nawo anthuwa? Mulibe mtendere ayudasi inu
Anali asanamugwilebe? Boma la zitsilu mmalo molimbana ndi ma real issues.... Bakili muluzi tv amawamvetsa kuwawa eti
Kodi mulibe zochita Zina Koma kusaka anthu oti akuuza amalawi zoona zenizeni anyapala inu zodiac idali kale BM TV is the best teacher
Wanzelu sangaombele mmanja zopepela zomwe ikupanga mcp zi.anthu tikuvutika kuti tipeze fertilizer chakudya chimene kulibe ndie mmalo mokonza mavutowa basi busy kusaka anthu omwe akuzuzulapo
Wodana ndi chilungamo ndi Adani a Bakili Mluzi tv
Bakili muluzi TV ndi ma comrade ena ngati limpopo fm, Born kalindo mukunana kwambiri simungapeze mungoononga ndalama pachabe 😂😂😂
Angofuna kubapo ndalama za amalawi panyapawonso
Kkkkkkkk Koma a Macra mukunama heavy tamangoban ndalamadzo not muzilimbana ndi bakili tv
Bakili muluzi ndi katundu mpakana 3.3 billion kugula makina kuti amusakire, ingogulani chimanga anthu asafe mwina avote nawo mu September muno
Machine emenewo akanakhal kuti alipo bwezi kwa America kulib umbamva ndi umbanda komas dziwani Mulungu amuteteza Bakili Muluzi TV ndpo adzafa kufuna kwa Mulungu pliz nthawi yatha iyi America akanakhal chisanzo koma ai machimo kumangochitabe shame
Iyo ndi njira yobera ndalama akudziwa kuti kwatsala kanthawi pang'ono mcp kuchoka muboma ndiye angagulile machine anzawo akulowa muboma posachedwapa.DPP ndi Boma kale.vakuba ivo
Izo ndy mbudxi bs ndimayesa akadakagula Ky chimanga otsati utsiru omwe akukambawo asalimbane ndi mumthu uyu iye amatidxiwira xowona
Kuba kopandanako manyazi chisekodi chawapana anthuwa sakupuma bwino adalakwitsa kumupha chilima kumeneko ndikupenga mitsala
Ndinjira yobela ndalama bwanji ndalama so osagulira mafuta akusowa
Mukucheza inuyo Mulungu sangalore zonyansa kuti zipitirire mdziko muno
😂😂😂 mangani boni kalindo kumalawi konko kapena mangochi kkkkkk makape mwaiwala kuti September yomwei mukuchoka
Vuto tilimu democracy ndiye sangampange munthu kusiya kudzudzula zoyipa
Osavotera mcp ndi yokupha,Kuba ndi kuzuza Malawi eni
Palibe machine amenewo akunama akufuna kugula machine obela chisango chifukwa ayesenza njira zobela mavoti akanika akunama kulibe amachine ogwila munthu pa social media akunama akufuna machine obela chisango patsiku lovota azagwirize kubela information patsikulo
zimenezo ndizimene zakupangitsani kuti mukanike kuyendetsa boma mumalimbana ndi anthu awiri atatu kusiya kuthandiza ma millions
Ndizokaikitsa kuti aguladi machine amewo. Komaso amalawi tisalore
Za manyi basi anthu akufa ndi njala
Kd mukamat agwidwa iye walakwa chan???
ayambe angula chimanga kaye 3:30
Kumalimbana ndi zinthu zopanda pake zinthu mmene zaduliramu
Agwila mapwala achakwera osati bakili muluzi TV machende amacra
Bwanji akulimbaba ndi bakili muluzi tv kusonyeza kuti bomamu muli kupakula komaso uchigawenga wakula ziko muno
Zaziii kungoononga ndarama ndizopanda ntchito , instead ndarama zimenezo bwezi mwapangira zinthu za phindu
Sanagwide pano watulutsa ina
Zinayamba kale kale izi koma mmmmm
Ndipo tikutchalenja kut angufuna kupeza njila yobela ndalama ,sangampeze wa Bakili TV
Ndie bwanji bon kalindo akukusiwa komwe akukara sakupitha akufuna kubha ndlama bass kkkkk kom ku malawi kokom
Funso akamugwira atani naye
Akunama alephela kumupeza Bakili muluzi TV.komaso tanyiwa.
Akunana padziko lapansi palibe matchini otelewa akungofuna kutibela misonkho yathu asatipusise komanso olo atachigula asadzinamize kuti angamupeze ntanyiwa ndi Bm tv anyamata amenewa amayidziwa kopyuta koopya ku mcp kulibe. Bm tv ndi ntanyiwa ndiomwe amatiuza zoona osati mbc ndipo ndiyomwe timavela history iz a best teacher
Mwayankhula broh
A Malawi nde tipindula nacho chani chi machine cho. Koma Boma la ku Malawi guys. 😂😂
Kkkkkkk achita bwino machine amenewa agwilitsa ntchito adzawo, tikhala ndi special 4n yothanilana ndi makapewa
Ndipo bakili TV ikulankhula zinthu ndima facts omwe ndiyeno mabozawo ndi ati anthu ophudzira koma Ali mbuli muubongo zosatira zake ndi zimenedzo
Ndekuti amanenadi zowona
Amacra analephera kulondora ndege ya chilima lero chifukwa alandira ndalama zakuba izi
Azatinamise ife akufuna kugula machine obela mavoti kodi machine ameneyo akunena kuti asigwira anthu otumisa uthenga wabodza akunama palibe machine amenewo akufuna kutinamisa awa akufuna kugula machine ovuvuta information yabela mavoti tsiku lovota ngakhale kwameleka kulibe machine amene akuguna kugula kwa merican anthu amayagula pazosho media
Koma tibeledwa myezi yasalayi...ife tipindula nazo bwanji..agulu awa atikwana bwanji
Akudana ndi Chilungamo
Boma likulephera kupereka ndalama kwa a Malawi omwe anapuma ntchito Zaka ziwiri ena zitatu zapitazo koma akufuna kugula Makina kugwirira anthu what a shame
Bakili muluzi tv is better than zodiac ndipo zimene akuchitazi ndizoipa achakwera mutu wawo siukugwila ndiye akuyese kufuna chochita kuti agwile munthu alephela
Mwa umbonda sizinga theke bakili TV ndi mbambande
Kokma chakwela uli ndi chikondi ndi anthu Malo mogula mankhwala chipatala kupanga zimenezo mulungu akuoneni
😅😅😅😅 inuyo kumugwila bakili tv inuyo Mr ntanyiwa 😂😂😂😂 nde bola ndalamazo mukanamangogula zitenge za MCP coz mwachepelatu kutali taliiiii ndipo 😅😅😅😅😅😅
chakwela ndichitsilu kwambili ndipo MCP ndichilombo. kukadakhala kuti silevo thiledi ikanalipo akanatigulitsa ndithu . uku ndikupha athu sakuyenela kugula mashiniwo bola chimanga.
Bodza lalikulu akufalitsa ndi chakwera, kumkuyu too much compromised
Ayamba kugwidwa ndi omweyo abomao koma Bakili Muluzi TV Mtanyiwa ndi akatundu mitunda ya phiri la Mulanje panchombo peni peni pa phiri lalitali la Mulanje zizivutani kuleka kuti mugule fetereza anthu anthire mminda mwao panopo chimanga chayamba Madera ena kumasula chopanda fetereza zopepera basi dziko la umasikini ngati linoli
Nkhani ndi yofuna kubisa Zinsinsi za boma pogwira anthu onena zoona za boma
Ndi njira yobela imeneyo
Akulimbana ndi zopusa .
Osapanga zogonjetsa njala ndikugula mankwala nzipatala ,komanso kupeputsa kudula kwazinthu m,dziko muno bwaa
No no no . Ndalama zisatuluke akunama awa.
Koma anthu akuseweretsa misonkho ya Malawi
Tinakuuzani kuti amene ali ndi vuto ndi Bakili Muluzi tv asamavele azangodwala nawo kunyu
Kodi iwowa anatiuza kuti tisamavele Bakili Muluzi tv iwowo chikhalilecho ali busy kuvela Bakili Muluzi tv
Kodi akugula machine pamene nthawi yawo yantha
Tikuvota posachedwapa chogulira machine ndi chani
Anthu enawa mutu umagwira
Kapena akugulira ife kuti tizawafufuze akazachoka m'boma
Kuti ali mudziko liti kapena chani
Sangagwidwe kudqna ndi chilungamo akufinyani simunati
Sanagule machini akunama akungofuna kwawopyeza anthu ndikwqnamiza ndalamayo aponya mthumba
Pamenepo ndipamene mziwe kuti mnasankha manyaka a presdent and his full squad cz malo mopanga zinthu zoti ziko lipedze mafuta komanso fertiliser ndi so njara yeti kumakhala busy ndi anthu omwe a kuwauza amalawi chilungamo zopusazi koma
Macra yachikangawa
Sangampeze agwanayo 😂😂😂😂
Koma mene akuvutikila anthu dziko muno mugakhale bz ndizimenezi
Emusipi ndiyamanyi Masalvage chipani chemenechi mchofunika kuchichita deregister and don't allow all it's top members kulowanso zipani zina,
Might be machine okhuza zachisankho basis,my view,angozembaisa
Zisiru zaathu agulu amenewa chakwera ndi onse omusatira
Kma kwa ine sizoona ayi akononge ndalama zambilimbili chifuka Cha muthumodzi azisiye zimenezi
Ndi zoonadi akusowa pobela ndalama za Malawi
Sangamugwile awonga ndalama ameneo
Agwa nayo😅😅
Machine omwe agulawo saphula kanthu bwanji alephera kuteteza Smartmatic yawoyo nde ngakhale agule machine amtundu ulionse padziko anthu ngophunzira kwambiri kuposa boma la mcp
Suleman kagwere ukoo ndi abale ako a mcp mukhaula sinati
😂😂😂😂Koma chakwela galu kobasi
Zamukanika Suleman 😂😂😂😂
Koma zitsilu izi za mcp mbuzi zaanthu😮
Kokolikoko wayabwidwa😅
Mcp ndi devil 😈 kupha, kuonga amusiye wa TV
Awa apa nzeru zatha njila zonse mwayesetsa koma vuto Satana nthawi zina amatopa, ndi Mulungu yekha saodzera satopanafe chikondi chake chimapita ponseponse, vomelezani basi kuti mwalephera iyi simfundo kugula cholinga ziwembu basi mupha angati? Basop Mulungu akakwiya ndithu mufa choima
Mukunama Mulungu awateteza
Zopanda ntchito, bakili muluzi TV si kape
Mbava anthu amenewa
Koma mitu yanu ikugwira?
Mmalo mogula Mafuta Anthu ma business ayima kusowa kwa Mafuta, Njala ili mbweeeee.
Boma lauchitsiru.
Akufuna kupakula CHAKWERA 😂😂😂😂 Koma yaaaaaaa MALAWI wanga