BON KALINDO LERO PA 25 AUGUST WATI VICE PRESIDENT MICHAEL USI WAGULITSA UTM KU MCP

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024

Комментарии • 123

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 19 дней назад +7

    Koma pali ndalama Palibe chisoni, apa anthu enanu mukuchita kuwonekera tu kuti mukhonza kupha m bale wanu chifukwa cha ndalama. Boni kalindo ife timamusapota chifukwa amanena chilungamo, amatiyimilira anthu osaukafe, akanakhala kuti ndi munthu opanda chilungamo, bwezi atadya chibanzi kale kale chifukwa anthu ena amamunyengerera ndi ndalama koma iye amakana. Bon kalindo is the best our president❤❤❤❤❤❤

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere 19 дней назад +1

      Sukudziwa kanthu iwe, akumanga nyumba Pano Chifukwa cha ndalama Zama bans zimene ukunenazo, uyu timakhala naye Ku machinjiri area 8 ngati ufuna Umboni ubwere tikakuonese Kwa njilika komwe akumanga nyumba

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 19 дней назад +10

    ❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Booooon kalindoooo 🔥

  • @AngolanChinga
    @AngolanChinga 19 дней назад +7

    Tiyankhulilen bs we love you always

  • @user-sm6pr9cg2q
    @user-sm6pr9cg2q 19 дней назад +3

    Ndizovala za utm sikut anthuwo nda utm , MCP ikuva kuwawa kwambili coz sizomwe amayembekezera

  • @ElizabethAlick-e6b
    @ElizabethAlick-e6b 19 дней назад +6

    Pitirizani kuyima pachilungamo bwana.

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 19 дней назад +3

    President wathu ife anthu osaukafe.Manganya ndi Yudasi yemwe anamupeleka SKC.kwa Lazaro.

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 19 дней назад +2

    Kodi Chakwerayu chomwe akufuna ndichani anamupha SKC. Koma pano akudana nayebe .Ambuye atithandize ndithu ndipo alowelerepo.

  • @MilikaKilion-tn1bn
    @MilikaKilion-tn1bn 19 дней назад +4

    Zosezi ndi ndi mamganya kamuthu koipa kapeneka

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 19 дней назад +3

    Manganya ndi masterminder wa imfa ya Chilima

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 19 дней назад +3

    Palibe amene angagulitse UTM ukunama ,,,,,,

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 19 дней назад +2

    Manganya anatenga nawo mbali yopha Chilima kumene zimachita kuwoneka ndi timaso take twani twani olo kuyankhula po pangozi zinachitika ija shame Mr zakeyu

  • @EmmaChimoto
    @EmmaChimoto 18 дней назад +1

    Ndiye mumafuna athu asauke chifukwa chani aaaa moyo wa masiku ano ndikokera kwako aripo angakane ndarama apa olo bonikalindoyo sangayikane

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 19 дней назад +2

    Wa UTM MENE APHELA CHILIMA. MUJA ANGAYIMBILA.MANJA FITI ANTHU AWA A MCP DZOSEDZI CHISILU MANGANYA APA NDIPAMENE PAKUDZIWIKA KUTI MANGANYA ANATENGAPO GAWO KUPHA CHILIMA AAAA KOMA MENE ACHITILEMO KAYA UTM ITHA KOMABE MCP 2025 TITHANA NAYO KULAMULILA MALAWI AYI ANTHU OWONONGA AWA

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 19 дней назад +2

    mulomwe ozelezeka lwe kulongolola ngati mzimayi

    • @PhillspicJere
      @PhillspicJere 19 дней назад

      Muhlomwe chisiru uyu akuoneka kuti uhlomwe wake ndiwaku Mozambique eeeeeeh satopa ndikulongolora

  • @augustMag
    @augustMag 18 дней назад

    The DC Boooon Kalindo the truth and justice speech 🔥🔥❤❤

  • @ChimwemweJuwao
    @ChimwemweJuwao 17 дней назад

    Bwana mtendere simuzaupezaso even mutazasiya pansi udindo simuzarandila uremu chifukwa moyo wanu anthu awuona

  • @Yaqub-nk4pu
    @Yaqub-nk4pu 19 дней назад +3

    Utm ipange zotheka kumuletsa Manganya kuchititsa msokhano in the name of utm other wise Manganya agendedwe

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 19 дней назад +2

    Opusa ndi amene alondola manganya

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 19 дней назад +1

    Iwe UTM SIINGAGULITSIDWE NEVER NEVER AKUGULITSIDWA NDI ANTHUWO

  • @GodwinNdekhantani
    @GodwinNdekhantani 17 дней назад

    Mwagula chipani osati mitima ya anthu ife sitingapite ku MCP ngakhale panti atasandusidwa kabudula

  • @DavieChisale-w1z
    @DavieChisale-w1z 18 дней назад

    Omwe akuvala za UTM nkumapita ku MCP asiye zimenezo

  • @GladesMhango
    @GladesMhango 19 дней назад +1

    Ena sinu a UTM Kalindo sukunama 😮

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 14 дней назад

    Ubwino wake iweso ukudya ndalama zopatsidwa kuchokela kwa anthu akukutumawo, ndani samadziwa kuti iweyo ndi wa dpp

  • @WatsonMsukwa-y5i
    @WatsonMsukwa-y5i 18 дней назад

    Ok

  • @WatsonMsukwa-y5i
    @WatsonMsukwa-y5i 18 дней назад

    Iwe kalindo umanena chilungamo

  • @mansonchinkhuzi
    @mansonchinkhuzi 18 дней назад

    Ndiwo ubale weniweni otukula dziko zabodza izi osadzigwiritsa ntchito

  • @amosnyirenda-pl1ss
    @amosnyirenda-pl1ss 18 дней назад +1

    nose ndinu zisilu kuvela chisilu chizanu chi

  • @CHIFUNDOCHINA-lp9lg
    @CHIFUNDOCHINA-lp9lg 18 дней назад

    NDIPO USI 😭😭😭😭 WAMPELEKA NZAKE

  • @AkimKollen
    @AkimKollen 17 дней назад

    Zowonadi bon kalindo

  • @kadijachilwan967
    @kadijachilwan967 17 дней назад

    Kodi Imfa ya Chirima muzipangira campaign

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t 17 дней назад

    -Kung'alura mopanda mantha kumene

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 18 дней назад

    Kafukufuku waonetsa kuti D.P.P 2025 boma

  • @LaitoneJefitala
    @LaitoneJefitala 18 дней назад

    Chisiru Bon Kalindo

  • @FabregasNdumba
    @FabregasNdumba 17 дней назад

    Boni kalindo nd chounikira changa

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 18 дней назад

    We are proud of u kalindo

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 19 дней назад +2

    KUPANDA KUTERO OSAWSPATSA MPATA CHAKWERA NDI MANGANYA MUDZIKO MUNO APA NDIYE ZAWONETSADI KUTI MANGANYA ANALI MGULU LAKUPHA NAWO CHILIMA

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 18 дней назад

    UTM si ya Catholic koma msogoleli wake was a Catholic member

  • @PreciousLesani-c2x
    @PreciousLesani-c2x 18 дней назад

    Apule nawoni tixiwe

  • @GegeJazola
    @GegeJazola 18 дней назад

    Makape

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 18 дней назад

    ❤❤❤❤❤

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow 18 дней назад

    Akulu UTM sichipani koma kaganizidwe sangatigule musavutike ata!

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 18 дней назад

    Ndizoonadi yagulitsidwadi ndili ndi umboni gyz U.T.M yathapodi zosadabwitsa yudasi anapeleka yesu chilima may u soul rest in peace

  • @user-vf2fo1mb2c
    @user-vf2fo1mb2c 18 дней назад

    Yeah money is a problem

  • @lytonmaseko4534
    @lytonmaseko4534 18 дней назад

    Boniiiiiiii k the Dc❤❤❤❤

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 17 дней назад

    Manganya ndi joker wa imfa ya chilima

  • @RichardChaomba
    @RichardChaomba 18 дней назад

    kalindo ndiwa DPP

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 18 дней назад

    Usi satana yunda sikaliotiii

  • @NaomiMagoha-uw7rm
    @NaomiMagoha-uw7rm 18 дней назад

    Akangopanga convention a utm, tione mmene zikhalire tisamangovera zopanda pale bwanji asatanawo osawatchula maina kupatula yemwe tikumudziwa kaleyo

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 18 дней назад

    adzagonjetsa ndi mphamvu ya ku madzi

  • @GegeJazola
    @GegeJazola 18 дней назад

    Bon kalindo on fire

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 18 дней назад

    Ana a satana awa MCP chipani cha satanic ichi nonse amene mudavotele MCP ndinu dzisilu mwationongela dziko tionana 2025

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 19 дней назад

    Amenewa Si a UTM ndi MCP yangovala zivala za UTM

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 19 дней назад

    Nonse amene mwatuluka ku utm ndipo mupita ku mcp mzimu wa chilima ukukanteni

  • @GiftDamiano-h4k
    @GiftDamiano-h4k 18 дней назад

    Musamachuluse zichewa zowonjezera kapena kuti zokomesera,
    Muzingopita papoint yeniyeniyo basi

  • @user-xt2gu9yt9q
    @user-xt2gu9yt9q 19 дней назад

    Ndipo ndizoona Ife timadabwa amanganya ndichani koseko kufuna ndalama muyaluka koma simungaphe utm koma ili ndiziko muziona mwamba mwathambo tiyamika mukukathani ndipo ndikusavuka bwino akabwila tiyenaoni Ife phe pa gabiloni

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 19 дней назад +1

    KUMIPEZA MANGANYA AKUCHITSA MSONKHONO MENYANI NDICHITSILU PAKUFUNIKA MANGANYA APEZE MAVITO MDZIKO MUNO NDIMUNTHU MODZI ANAPHANAWO CHILIMA MANGANYA MWAZIEONA TIYENI TIKUTHE MANGANYA AMALAWI NDI KAMBERE MBERE

  • @WatsonMsukwa-y5i
    @WatsonMsukwa-y5i 18 дней назад

    Koyipa

  • @LeonardDavid-tc5iv
    @LeonardDavid-tc5iv 19 дней назад

    Zoona bwana

  • @user-sm6pr9cg2q
    @user-sm6pr9cg2q 18 дней назад

    Koma ukhala uchitsilu wa usi chifukwa MCP ili ndi vp wake kale ndi thawi yot akanamanga chipani chawo

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 19 дней назад

    utm siinagulisidwepo and utm siingagulitsidwepo never

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 19 дней назад

    Movement sigulitsidwa

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o 19 дней назад

    Tangoyambisan chipan chanu a kalindo

  • @matthewmathotho1238
    @matthewmathotho1238 18 дней назад

    Tipaseni ma hint who they’re

  • @user-ig9qk6gi6g
    @user-ig9qk6gi6g 19 дней назад

    Manganya chitsiru kwambili,

  • @PatrequeLequinala
    @PatrequeLequinala 19 дней назад

    ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 19 дней назад

    MANYANYA ATAWAMO MUNO MALAWI ATATENGERE ZIBWANA OLO KUFA KUMENE

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 19 дней назад

    Pangolini kuyankhula mosaopa

  • @nesposhi
    @nesposhi 19 дней назад

    Yudas wooneka ndi maso

  • @ZelipaMalanda
    @ZelipaMalanda 18 дней назад

    Kalindo chamba chidamupweteka. He is mentally ill. Opusanso ndi anthu omwe akutengeka nayewo, mnzawo ndi ntchito imeneyi akudyerapo mwana wa adad, zochita zopezera ndalama zikumusowa, akudyera momwemu. Amangondimvetsa chisoni kuti sukulu siidamupindulire. Timanena kuti sukulu imangochotsako umbuli wokha siichotsa uchitsiru koma zimandimvetsa chisoni kuti Kalindo siidamuchotse ndi umbuli womwe; zonse umbuli ndi uchitsiru zidamutsalira Kalindo sukulu siidamupindulire adakangotayako ndalama. Ndalama ankalipirira fizizo mwina akanangoyambira bizinezi kapena kuzilowetsa kumunda bwenzi ali pena, sibwenzi akavutika ndi zopusa akuchita panozi ayi.

  • @RaphaelWinford-ot9ct
    @RaphaelWinford-ot9ct 19 дней назад

    😮😮😮😮😮😮😮😮

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma 18 дней назад

    Ndipo kalindo umandinyasa olo ndimau omwe anakumana

  • @HendersonNambera
    @HendersonNambera 19 дней назад +1

    Ndipo live jisse ndibuli zooondi

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 19 дней назад

    CHIMENE CHIKUFUNIKA KWAMBILI LIPOTI LA NDEGE LITULUKE MWACHULUKA CHIBWANA MUDZIKO MUNO

  • @ChikuMega
    @ChikuMega 19 дней назад

    Guys muzikha ndi zeru muwone aliyese kumneko angovala ma glass muziwe kt imneyo ndye satanic yaxungulila

  • @RuthMkangala
    @RuthMkangala 19 дней назад

    Komatu wina apusa nazo izi

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 19 дней назад

    Galu iwe za ziiiiiiiii ndi jealous yakoyo

  • @ChifundoNkhoma-x7p
    @ChifundoNkhoma-x7p 19 дней назад

    Iwe chifundo samakhala opanda zelu usinthe dzinalo , iwe unthan kumpha mwana wako chifukwa chandram zovetsa chison.

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 дней назад

    Kkkk a matchalitchi chikuwagunda ndichani uyaluka winiko matako ako

    • @BFWCPHIRI1978
      @BFWCPHIRI1978 19 дней назад

      Iweyo ndie akuchita kuonekeratu kut iweyo ndi mmodzi wa chikangawa satanic party koma nonse munya 2025

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 18 дней назад

      Akugwetsani asatanic mukwele galimoto mawali umfa

  • @HappyBlackberries-ql9uo
    @HappyBlackberries-ql9uo 18 дней назад

    L

  • @JohnMsakambewa
    @JohnMsakambewa 19 дней назад

    Kalindo umbuli ukumuzuza zedi ngati sudziwa kathu ungokhala Basi ulila mpaka liti?

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 19 дней назад

    Usasokoneze maganizo anthu ndi nkhani zako zonamazo Nonsense,,,Wekha ukunena akuvala ma t shirt ndi a Mcp

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 19 дней назад

    Kaya UTM yagulitsidwa kaya ai Ife sizikutinkhudza, izoso ndizawo, chomwe tikudziwa nchakuti andale ndiamodzi. Iweyo born kalindo ngat Uli munthu oima pachilungamo n siupanga zandale, n'chifukwa chani umakamba zandale? Ndie ingoima ndiweyo ukhale president ndiweyo udzayendetse dzikoli osati uzingotiuza zopusazi chifukwa ndiwe yemwe unkanyoza DPP nkuwatsogolere anthu ku MCP n lero ukunyozaso MCP nkumawatsogolera anthu ku DPP komwekuja, kod amalawife mumafuna kutitenga ngat zitsiru? Kupusa

    • @KhooMadex
      @KhooMadex 19 дней назад

      Mbuzi iwe kodi ukuti chani, tayankhula zonveka

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 19 дней назад

      @@KhooMadex mbuzi ndi amako aise

    • @isaacchiwaula731
      @isaacchiwaula731 19 дней назад

      @@KhooMadex ngat siunanve nkhala nkusanva kwakoko popeza ndiwe gonthi nchifukwa chake siunva

    • @corretabanda7685
      @corretabanda7685 18 дней назад

      A Bon a Chilima alimoyo ankati ndiwopusa, lelo akuti anali wanzeru timve ziti

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 19 дней назад

    MANGANYA MASENDE YAMAKO TIRHANA NAWE

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 дней назад

    Iweyo ungakane galimoto chitsilu iwetu

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 19 дней назад

    Pambuyo panu bwana

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o 19 дней назад

    Ndan asakonde ndalama wausiru iwe

    • @user-vw4hj1co9f
      @user-vw4hj1co9f 19 дней назад

      Aaa iweyo uthadi kupeleka mai ako chifukwa cha ndalama asatanik inu unya

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 18 дней назад

      Idya ndalamazo koma ndizasatanic uzingomwalira ayise

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 19 дней назад

    Ife monga akubanja tikuti pepani munthuyu anadwalako misala akuyenda ndi ma paper aku mental ndiye zonse zomwe akulankhulazo ndizamisala, muziona amangolumikiza nkhani zopanda mutu zosadziwa kuti akupita nayo kuti, pepani aMalawi munthu ndiwamisala uyu

  • @HellenChimwaza
    @HellenChimwaza 19 дней назад

    Iwe unatikwana ndi mau ako onyasawo

    • @JamesMhango-w2q
      @JamesMhango-w2q 19 дней назад

      Ndiwe chitsilu kwambiri ungamunene kalindo moteromo uzikhala ndi umunthu mene akuphera chakwelamu ungamayakhule Zoputsa

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 18 дней назад

      Musiyeni akakwela galimoto upita ndi asatanic akugwetsa

  • @SimpsonGerald-j4x
    @SimpsonGerald-j4x 19 дней назад

    Ndiye iweyo Bon kaliwondewonde chikukhudza ndichani ngati chipanicho nchakwanu

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg 19 дней назад

    Ana achikangawa awa asakuziwa ndan

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 дней назад

    Kkkkk atagendeyo ndani machende ako

  • @LovelyDumplings-yf7pd
    @LovelyDumplings-yf7pd 19 дней назад

    Kalindo ndiwaboza iiiiii

  • @cjaymw496
    @cjaymw496 19 дней назад

    I blame manganya

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 19 дней назад

    Akalindo, doda la boza ili

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 дней назад

    Kalindo. Chitsilu iwe mesa naweso ukulandila ndalama ku DPP ndiye ukufuna kuti azako asadye money

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 19 дней назад

    ❤❤❤❤