Zikom kwambiri Bon Kalindo pajatu mau amati aneneli bodza muzawaziwa ndi ntchito,zawo,ndiye amenewo ,koma dziko li mene likuyendera, anga muuze chakwera kuti,dzikoli likuyenda.bwin,mugoziwiratu kuti ana a njoka awa, akunenepas mimba zo, kodi or chakwera payekha,sakudziwa kuti dzikoli li pamavuto, God bless you .we love you, the DC.
Mr born kalindo, apa mukundimvekera bwino kwambir,pankhani ya ma estate akumalanje,thyolo ,mdakonda kufunika kuguwa Malo amenewo kuwanthu wamba ,efe tea ameneyo sakutipindulira, , Malo amenewo
The dcccccccc mundipasire moni kwa fada vini wandale I miss him, program komzani tikalime kalongonda mmenemo nthaka ya ku thyolo chimanga chingotsandu pano. Land yabwino mkumeneko ku tea ko🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️
Kupatulapo ineyo siine kape ineyo papa prophet B macheso sikape makape ndiamene akumapepha azibusa ndiye makape koma ineyo papa prophet B macheso sikape APM boma basi
The DC muwauzeso a minister azayendele Jibs security company ku Blantyre akuzuza anthu awo, amadula anthu ma 10 000 mk aliyense every month akafutsa amawauza kuti ndi ya uniform, akadwala amawadula ndalama, payment imachedwaso kubwela , ndi zambiri zili kumeneko

Mumatiimilira aborn kalindo keep it up
❤ The DC your the best
True leader, Zikomo Honourable Bon Kalindo ,you tell the truth abd stand for the people ❤❤❤❤May God keep you safe
Boooooon kalindoooooooo the Dc❤❤
Mr kalindo machine operator 💪💪
Freedom fighter of malawi Mr born kalindo
The.DC chimwana chovuta mulungu azikusunga kt uzitiimilila
😅😅😅mitu yawo siikungwila amenewo ,asata bwino ,akhaula adabwa gatilili dyela ayaluka adabwa
The number one man of the moment
Amene amapita ku state house especially Azibusa ukunena zoona Mr DC ndi makepedi osusuka kufuna ndalama
😂😂😂😂😂 Kom ichi ndimamuna kwambiri kkkk
1st president wa anthu osauka muno m'malawi❤
Na zakumakanjiradzo akanatiganizila anthu akufela ndikubwelekera njira akatimizidwa kuchipatala ky chakumangochi ky kusalilma 💔💔💔💔
The DC president wathu osauka mulungu azikudalisani
I can live you Mr bon kalindo
Mr born kalindo, apa mukundimvekera bwino kwambir,pankhani ya ma estate akumalanje,thyolo ,mdakonda kufunika kuguwa Malo amenewo kuwanthu wamba ,efe tea ameneyo sakutipindulira, , Malo amenewo
The last man standing indeed,THE DC🎉🎉🎉🎉
More fire Fada
Awuze the DC osati you nyo nyo nyo boma ndi lomweli lachanidi? Big up the president
Dc katundu inuyo boss ❤❤😂😂
waganyu,oyamba,ndikalindo,
Mnyamata wa kwa Njeza ang'aluleni bas nthawi yawo yatha
The dcccccccc mundipasire moni kwa fada vini wandale I miss him, program komzani tikalime kalongonda mmenemo nthaka ya ku thyolo chimanga chingotsandu pano. Land yabwino mkumeneko ku tea ko🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️🏋️
The DC...mwana wachabe kwambili 🔥🔥
@vitumbiko Mumba. Pitani ndithu ku Lijeru tea anthu achosedwako ntchito
The DC mwana woopya kwambiri akufuna kupanga mademo anyo kuswa kuswa😅
From njeza village T/A mabuka box 76, mulanje Malawi southern Africa.....😮
The DC man of the moment
Nyonyonyo !!😂😂
Avitumbiko tabwera I ku dpp muweke bhoo vepi yanu ndimakufini man mubadwira amalawi inuyo
Zowona DC God bless you
Kupatulapo ineyo siine kape ineyo papa prophet B macheso sikape makape ndiamene akumapepha azibusa ndiye makape koma ineyo papa prophet B macheso sikape APM boma basi
Katundu waboma uyu
Ife ndife a Malawi iyini ake a nthaka kubadwa tabadwila konkuno kukulilanso komwekuno palibe angatiwopseze
Ku lujeri bwana wina akumalemba anthu ntchito 4;koloko am nde anthu kuwopa kuchedwa akumagonera konko😊
Ambuye azibusa oterewa muwakhaulitse cifukwa comwe akucita saziwa enawo sanaitanidwe
Kkkkk akuti olochakwela ndinazamuuzapo 😂😂😂😂
Imagine
katundu muzinthu❤❤❤❤
Ambuye Mulungu wonani Malawi mwapa dera 😭😭😭
Mmakwana inuuu mutiphula mavutoo??
Dyera asogoleri zelu alibe
Azibusa accp ndi adyera ,amakudya heavy
Tea timutchetchamo aonanso
Aaa adzibutsa enawa agalu KWABASI
Dc you deserve ❤❤❤❤
The DC akatundu
The DC muwauzeso a minister azayendele Jibs security company ku Blantyre akuzuza anthu awo, amadula anthu ma 10 000 mk aliyense every month akafutsa amawauza kuti ndi ya uniform, akadwala amawadula ndalama, payment imachedwaso kubwela , ndi zambiri zili kumeneko
Zoonadi the dc freedom fight wathu
😂😂😂 akatundu awa
Azibusa asatanik amenewo , anamachende zitsiru zachisatana
DC ulemu wanuu
😂😂😂😂😂😂 ati opemphera Koma makape okha okha
The DC ❤
Zaphavu ❤❤❤❤
Tilinanu Mr DC
koma Andu if Mmmm zot mavuto amenewa Kut azatha kumalawi ndakayila
a,dpp,lelo,mwakumbukana,,,,ulungu,,,,,mwaiwala,muja,mumatukwanila,muja,mulungu,sakodwa,ndimuthu,otukwana,onamizila,bodza,anzao,ndipo,dpp,singawine,izo,mudziwe,
The Dc❤❤❤
osasekelela agaluamenewa born kalijdo
awaso,ndachitsilu,akuona,ngat,angafanane,ndi,usi,boni,kalindo,akufa,ndimaganyu,otukwana,boma,pano,usi,silevo,yake,
kalindo,ngakhale,atanama,,,,,,bodza,kulinamizila,,mcp,adzakhumudwa,mcp,itawinaso,
Talk talk,talk❤❤❤❤
Azibusa omvetsa chisoni
Bola Inu Osati Bakili Muluzi Tv
Ukhaula kwambiri😂😂😂😂😂
❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤
Don't shout at the clergy Mr Bon Kalindo just advise them otherwise hmmmm
Ndipo ndipo kuli mulungu kunja kuno
Chaka chino tikusintha bola osaopa
❤❤❤❤❤❤MR DC
Ndipo asadzafe
❤
Mumakwana fada iponden basi
Double tap to hear this voice note
▶︎•|၊|။||||။၊|။|||။|||02:55
DC not ng'anga but ng'onga
Dolo kwambiri
Afumu makanjila nawo amangotengeka kulikonse
Pastor ali after money shame malawi
Zitsilu za ccap
Nyooooo
ruclips.net/video/o0g35X9MOE0/видео.htmlfeature=shared
,iweyo,ulimbikile,ganyu,yomatukwana,boma kt,ukhale,nindalama,zambili
The last man standing dc
The DC
The DC ❤❤❤❤
The dc
Fire fire 🔥🔥🔥🔥🔥 the D.C
🔥
The DCccccccccc
The DC...mwana wachabe kwambili 🔥🔥
The DC ❤❤❤❤
❤❤❤
❤❤❤❤❤❤❤❤
Mumakwana fada iponden basi
ruclips.net/video/o0g35X9MOE0/видео.htmlfeature=shared