Symon & Kendall - Simungayime Ndi A Chakwera Mwachepa (Visualiser)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 ноя 2024

Комментарии • 89

  • @ThunileKawonga
    @ThunileKawonga Месяц назад +2

    Ndine wa opposition Koma eeh nyimbo mwakwapula🔥

  • @BesterWilliam-y3y
    @BesterWilliam-y3y Месяц назад +1

    Boma ndilomweli sitikusitha more fire🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @IndoliNyirenda
    @IndoliNyirenda Месяц назад +2

    Awa ndeeee ine zomwe amapanga zimandinyasa hvy Kaya ndi umbuli wanga uwu

  • @SamalaKadzamila
    @SamalaKadzamila 10 дней назад

    Agalu kwabasi kodi agaluwa ndiambili

  • @OlivaPhiri
    @OlivaPhiri Месяц назад +2

    Chinyimbo chanyoooo

  • @CarolyneGunda
    @CarolyneGunda Месяц назад +5

    Kodi izizi mumati ndikuyimba kapena magule, awa samatha kuimba

    • @edgarmax-pi1bx
      @edgarmax-pi1bx Месяц назад +1

      Taimbani lnuo tivere yanu ngati mungakaimbe pa condecer paja uribe zeru nyapako wava

  • @rajivjere110
    @rajivjere110 Месяц назад +2

    Kumenya kupha chi nyimbo 🔥🔥🔥🔥

  • @JoshuajuniorNkosi-b3u
    @JoshuajuniorNkosi-b3u Месяц назад +1

    kkkkkkkkkkkkkkk kuti pusika tawatumbuka yay ndindayowoyepooo ivoooo kutizgerezgeska yay vichewa imweeeeeee

  • @BrightZionga
    @BrightZionga Месяц назад +5

    Tizitsilu tinanso iti tianthu ta dyela

  • @MackzainWhite-rj9tx
    @MackzainWhite-rj9tx 8 дней назад

    Umphawi ndumene ukukupangitsa anyawu ine kuti mudzimuyimbira nyimbo ameneyo mbudzi za anthu inu mukhumudwa 2025 poti masiku atsala ochepa 🤘

    • @RonaldMakamo-hw7un
      @RonaldMakamo-hw7un 5 дней назад

      Agaru inu boma kulibe kusintha mupakana 2030 woooooo

  • @ThunileKawonga
    @ThunileKawonga Месяц назад

    Nyimbo ili bho Koma ❤💙

  • @YusufAjida-t8r
    @YusufAjida-t8r Месяц назад +1

    Bas ikakhala yakuvutani ya ndiwo kuthamamda chikangangawa tikuchapila limodzi 2025 tizinda ife zimenezo agalu inu chamba eti

  • @NelsonKameme-sy2vy
    @NelsonKameme-sy2vy Месяц назад

    CL touch production Iyiyi ndi ma rolling ake tinawaloweza

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj Месяц назад +3

    Kkkkkkkkkkkkk koma kumalawi iiii chinyimbochi achewa avutanacho zoti akugona osadya kuwililatu

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 Месяц назад +1

      Achewa akudya aise😂😂😂😂😂 alomwe ndi amene akudya chitedze sorry man timalima kuno sitidalilaso fertiliser otchipa

    • @KondwaniBanda-ul8sj
      @KondwaniBanda-ul8sj Месяц назад

      @@wisdom20mkango49 kkkkkkkkkkkkk moti inu mukusangalala zedi ndi ulamulilo o tate

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 Месяц назад

      @@KondwaniBanda-ul8sj baba usi says Malawi ndi munyumba mwakomo.... Every government has its own advantage and disadvantage, ndiye no kuti zizingoti atele ayi mwakuti na let's just work mwatokha basi.... We are t the end days so mavuto wa kupanda kuwadyera mutu mmmmh

    • @KondwaniBanda-ul8sj
      @KondwaniBanda-ul8sj Месяц назад

      @@wisdom20mkango49 mafuta agalimoto amalandilisa aulele mesa timagula ngati bomba labwelesa mafutawo NDE Malawi wanyumba mwanuyo mumakavotelanji zipatala makhwala sakupezeka athu osauka akuluza miyoyo chosecho voti yamuthu osaukayo inapanjitsa wina kukhala paulemelelo

  • @lydiakansuwe27
    @lydiakansuwe27 Месяц назад

    Tuvina basi shaaaa kwavuta.....😂❤

  • @StanielPeter
    @StanielPeter Месяц назад

    Babande

  • @jeremiahmalikebu2393
    @jeremiahmalikebu2393 Месяц назад

    Koma penapake sakundimvekera ngati Symon & Kendle omwe tikuwadziwa wa

  • @MATHEWSMALITINO
    @MATHEWSMALITINO Месяц назад

    Mbambande nyimbo ndipo ine ndi mphata leni leni

  • @chrissychamveka
    @chrissychamveka Месяц назад

    Wow nice song

  • @GodfreyKamphiripiri
    @GodfreyKamphiripiri Месяц назад +2

    Nyau Nyau nyau

  • @mikeasmachine4581
    @mikeasmachine4581 Месяц назад

    Asandichimwitse src

  • @RonaldMakamo-hw7un
    @RonaldMakamo-hw7un 5 дней назад

    Mukunamatu inu anamwalira nda wanthu adakali moyo mwina ida walira ndi nkhalamba yanuyo yopanda mano nkamwa

  • @MisheckChiwaya-ev6rr
    @MisheckChiwaya-ev6rr 19 дней назад

    Wachepa kadet

  • @WatsonMalanga
    @WatsonMalanga Месяц назад +2

    Amphawi achabechabe inu chokaaaaaa

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo Месяц назад

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @mannassehchikuni
    @mannassehchikuni Месяц назад

    Kma a2 akufa ndi nsanje,, Chakwera akadzawina ena adzakomokaa

  • @ElijahTheprophet-y9m
    @ElijahTheprophet-y9m Месяц назад +2

    Palibe chomwe ndanva kodi akuti chani?

    • @ThandiShandu-l6w
      @ThandiShandu-l6w Месяц назад

      Obwera kwanu ku Mozambique ukumva bwanji ndomalawitu awa kubandula DPP

  • @RonaldMakamo-hw7un
    @RonaldMakamo-hw7un 5 дней назад

    Ku opposition ndi kumandadi

  • @DziyaMwale
    @DziyaMwale Месяц назад

    kumenya ku gwetsa

  • @ChristopherKatola-g6p
    @ChristopherKatola-g6p Месяц назад

    Km mwagagada eeee

  • @RonaldMakamo-hw7un
    @RonaldMakamo-hw7un 5 дней назад

    Kulibe kusintha boma

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell Месяц назад

    Aaaaaa president wabwanj omat anthu kungokuva kut wamwalila aliyese kusangalala muziziwe kut simuli bwino muzawinila kubela ma vote bas osat chilungamo ay

    • @AckimKachiluwe
      @AckimKachiluwe Месяц назад +1

      Kmatu ndimene zilili or zikuoneka kuti boma silili bwino kmano APM unja ayi khalamba apume Muthu unja nde bola yemwei azitizusabe until wanzeru wina azapezeke chiyembekezo chinali mwa Skc emwe unja basi kma zinazi ayi ndithu

    • @Banana-o1r
      @Banana-o1r Месяц назад +1

      Musamati aliyese. Osamaphatikiza enafe uziti iweyo unasangalala

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v Месяц назад

    Eyaa sitisitha boma lomweli tingositha president zakachaso basi

  • @LazarousNamakhwa
    @LazarousNamakhwa Месяц назад

    Anthu omvesa chisoni inu dziko likupita ku mpompho ili

  • @frankndawandawa6666
    @frankndawandawa6666 Месяц назад

    Nde oimba onse agudwa koma kuli ntchito koma ubwino wake ovota sioyimba okha okha 😂

  • @NthawiKatanga
    @NthawiKatanga Месяц назад +1

    Mwagudwa zisilu zawanthu ndalama zamagazi

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo Месяц назад

    Tinvere zimenezi

  • @sweeneykamwendo6251
    @sweeneykamwendo6251 Месяц назад

    Boma silisinthidwa timasintha pulezidenti...2025 zitheka ndithu

  • @LazarusMpinganjira
    @LazarusMpinganjira Месяц назад +1

    Mbambande kadet mutu sukuweka

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge Месяц назад

    Asay ndi akendal mukunama anawina chifukwa cha chilima mwayiwala mapeto Ake mkumupha

  • @AcksensioChikondi
    @AcksensioChikondi Месяц назад

    Macadet akapuma kumandaa BOMA ndilomweli la MCP 🔥

  • @RawrenSonga
    @RawrenSonga Месяц назад

    Chinyimbo mwampha anyamata ichi kkkkkkk ku opposition mkudzuwadi😅😅😅😅

  • @ChancyWilly
    @ChancyWilly Месяц назад

    Mukunama inuyo oimba ndale simukuziwa munkhumudwa

  • @Martinmkapangakapanga
    @Martinmkapangakapanga Месяц назад

    koma anthu osayimbako za mulungu ayi koma za campeni basi ayi zikomo muzatenge ndalama popita kumamda ubwino wake ananena kale mau fumu onse azantha kuzakhala 😢😢😢

    • @MaupoChibwe
      @MaupoChibwe 14 дней назад

      Suwawona oyimba za uzimu? Why not going there and listen them .

  • @YohanePaul
    @YohanePaul Месяц назад

    Nthawi zonse kumangoimba za gule basi aaah zaziii imeneyi ndi nyimbo?

  • @SamuelChikomo-ox9ll
    @SamuelChikomo-ox9ll Месяц назад

    Produced by viwe

  • @RonaldMakamo-hw7un
    @RonaldMakamo-hw7un 5 дней назад

    Tawonani galju wanu uja mumati namiwa alikutiko adathawa mafuso zina ungoyamba waziona, agalu inu a dpp ndi opposition yonse

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn Месяц назад

    Kumenya ndi kupha mbali imodzi ya ziwalo za bwana 😂 Dan lu anatelo

  • @DanielChinomba-f5z
    @DanielChinomba-f5z Месяц назад

    Bola azapezeke pa Barot

  • @robertdaud510
    @robertdaud510 Месяц назад

    Muli ndi nthawi yothithera bundle 😢😢😢😢😢

  • @RebeccaChikalenda
    @RebeccaChikalenda Месяц назад

    Nde mwatero kd lne kwanga ndi kuva

  • @gettona
    @gettona Месяц назад

    Boma ndi Lomweli

  • @ChancyDzinkambani
    @ChancyDzinkambani Месяц назад

    😂😂😂😂kunyetsa kugwetsa boma ndi lomweli

  • @BrownMatonyola-xi3lb
    @BrownMatonyola-xi3lb Месяц назад

    Kendo wa cashgate

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri Месяц назад

    Chakwera alibe saizi kharamba zogwa mkumina sizingamwke,boma ndi lomweri

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona Месяц назад

    Kodi anatigulanso iti 😂😂😂

  • @MustapherLino
    @MustapherLino Месяц назад

    Agalu awa Simon ndi kendel

  • @ChizzaNkhonjera-k8y
    @ChizzaNkhonjera-k8y Месяц назад

    Pitani koko mkadyeko ndrama zophwekazo

  • @InnocentMakira
    @InnocentMakira Месяц назад

    boma ndilomweli

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc Месяц назад

    Akaimila Ku garden city kkkkk malo moimba nyimbo yomupempherera wachepa ndi chakwerayo

    • @Halima-i4x
      @Halima-i4x Месяц назад

      ❤❤❤❤ ndipo et et 😅😅😅😅

  • @DesmondTaulaye
    @DesmondTaulaye Месяц назад

    Mbuli za anthu

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev Месяц назад

    Kulira Kuja kwatha agalu inu?

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Месяц назад

    Koma pa Malawi pano oyimba ngat Lucius Banda omayankhulira amalawi alipo???? Dyera will take you no where..

  • @mosesmachokero3068
    @mosesmachokero3068 Месяц назад

    2025 campaign kuli ntchito kkkkkkkkkk

  • @BeniNazombe
    @BeniNazombe Месяц назад

    And

  • @StonexLonjeMtaya
    @StonexLonjeMtaya Месяц назад +1

    Boma ndilomweli 🔥

  • @RabeccaChiumia
    @RabeccaChiumia Месяц назад

    Sinzaiwala amayi omwe anandiloza ku ukwati kuti uyu wadya kale .😂

    • @Josephiriillovo
      @Josephiriillovo Месяц назад

      Eeeehh halla me ndimve nkhani yonse ndithu😅😅😅😅

  • @DesmondTaulaye
    @DesmondTaulaye Месяц назад

    Kodi munawina panokha?

  • @FrancisLefton
    @FrancisLefton Месяц назад

    Dolo

  • @mariahmatto8182
    @mariahmatto8182 Месяц назад

    😂😂😂😂😂😂

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Месяц назад

    🤮🤮

  • @AmosShadreck
    @AmosShadreck Месяц назад +1

    Achewa opusa awa