BRIAN BANDA KUWELENGA NKHANI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 сен 2024

Комментарии • 97

  • @SkabhuKabhu
    @SkabhuKabhu 22 дня назад +8

    Kodi kuyeselela masango ziyamba chaka chino ifetu sikuyamba kuvota sitinamvepo zoyeselela masango zitheka bwanji

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 22 дня назад +3

    Don't worry guys, next year kaboma aka kakuturuka basi 😂😂😂 and sikazabweranso

  • @RachelNkhoma-vn2jo
    @RachelNkhoma-vn2jo 22 дня назад +5

    Mwaonatu umunthu alinawo anthu aku Malawi kupulumutsa anthu pa ngozi,funso mkumati Kwa Mr chikangawa ndi achina yudasi munakanika bwanji kuwapulumutsa a vice president ndi anthu ena ???

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f 22 дня назад +8

    Tangotsegulani kawundula olembetsa osati zomwe mukunena apa zoyesera.
    Maina omwe muyeserawo mutani nawo?
    Please ngati mukupita kuma church pangani chilungamo for the first time

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 22 дня назад +3

    Kod ayesela bwanji mmalo mongoyama..., zoyesazo ndie zitiso..,,, ndayamba kukaika guys

  • @kondwanisikatoleka7354
    @kondwanisikatoleka7354 22 дня назад +5

    Musalorere pliz...!!! Masankho sayeserera,, uku mkuba😢😢😢😢

  • @DysonKamama-yh7hq
    @DysonKamama-yh7hq 22 дня назад +3

    Zisankho samayeselela akufuna abele

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 22 дня назад +4

    Kalembera oyesera zichani zakuba bas kuyambira liti zimenezi gati ntchito simuntha osagonena bwanji mafilim anu tawadziwa

  • @user-tw9nl6ks9d
    @user-tw9nl6ks9d 22 дня назад +2

    Born kalindo anachenjeza kale izi azipani zotsutsa boma musafatse moonjeza akuberani zisankho mutu uli gwaaa

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o 22 дня назад +2

    Nthawi yoyeselela machine azisankho tilibe sitingaipeze, plz aChakwela ndi abale anu mutha kuwayesa nde mutiuze

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 22 дня назад +1

    Zachison kwambiri anthu akumwa madzi okuda chocho 😢😢😢😢 I wish ndikanakhala othekela kuthandiza ndikawakumbila mjigo boma lipangepo kanthu please please zililiso

  • @user-wd5tw1mz8h
    @user-wd5tw1mz8h 22 дня назад +3

    Chisankho sichimayeseledwa akufuna abele mavote, inu osusa musamale muzalila

  • @ThokozaniBondo-em9fr
    @ThokozaniBondo-em9fr 22 дня назад +2

    Tiwonepo bwino apa zinayamba zachitikapo zimenezo chibwana ichi anthu akuvutika dziko muno ndye muzipanga masewera anuwo

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 22 дня назад +2

    Pasapezeke Malawi opita kukavota zoyeselelazi plizzzz anthu awa afuna atiputsitse amalawi chondeeeee

  • @user-lw2yp1rf4n
    @user-lw2yp1rf4n 22 дня назад +5

    Zakuchikangawa zija sizinakwanile?😢😢😢😢

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 22 дня назад +1

    Ku Malawi nkhani ya kuvuta kwa madxi musaname kuti ndi chifukwa cha kuchuluka kwa anthu ayi nkhani ndi kusakhala ndi chidwi cha atsogoleli aundina wamadzi South Africa ili ndi anthu kuposa malawi koma simungamve nkhani yovuta kwa madzi ngati malawi nkhani malawi aphungu kuzikundikira

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 22 дня назад +2

    Ango funa kubela mavoti

  • @ManuelLifa-s9o
    @ManuelLifa-s9o 21 день назад

    Zisiru dzosavazo zapangisa kare

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 21 день назад

    Abrian banda komatu ngozi yathu ija alo modzi opolumuka anthu 9 awa adzathuwa bwanji anthu atatu kupulumuka modzi,plz tifusutsileni amw.

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 22 дня назад +3

    Ndiye ndege yanthu ija zinatheka bwanji kusapulumusa anthu 9 ajaa km achakwela😢😢😢😢😢😢😢😢 munamulakwila chilima

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 22 дня назад

    Tipanga mademo mukapanga xibwana

  • @SteviePatrick-g2p
    @SteviePatrick-g2p 22 дня назад

    Mankhwala osavomelezeka alokod

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 22 дня назад

    Denge ya chakwela igwa liti Eish 😂😂😂

  • @SteveriaNyalugwe
    @SteveriaNyalugwe 22 дня назад

    Akayenderenso dera la Mulanje Pasani mmudzi mwa Nkwaira anthu akyenda mtunda wa 3 kilometres kuti apedze madzi akumwa, anthu akumagona pa chitsime kudikilira madzi. Mijigo inawonongeka pomwe inawuma madzi sakutuluka. Mapaipi amadzi awaterboard anachotsa ndi cholinga choti anthu adzilipira ndikuika mapaipi awo, koma mapaipi awowo sakugwiranso ntchito. Anthu akuvutika kowopsa zikumaphweka kwa munthu yemwe ali ndi njinga koma amene alibe akumwa madzi adzithaphwi.

  • @InnohLukah.1998
    @InnohLukah.1998 22 дня назад +1

    Mmalo moti igwe ndege ya chakwera 😂😂😂😂

  • @user-yg4zv4qd2l
    @user-yg4zv4qd2l 22 дня назад +2

    Koma Dpp idakhala zambiri osawapatsako mijigo mmaderawa.

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 22 дня назад

    Zoyeserazo ayesele pa anthu 10 okha zinazo mzanong'onedza bondo

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 22 дня назад

    Akufuna kuyesela kubela mavote agalu amenewa

  • @ShalifuMatola
    @ShalifuMatola 21 день назад

    Mukutimwesa za boza

  • @NAKHWAIYANA
    @NAKHWAIYANA 21 день назад +1

    Timenyanatu, from when? Why you didn't imform as before zakuvutani then muti timayesela zida fosek

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira 22 дня назад

    Bodza akufuna kubera

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v 22 дня назад +1

    Kuyeselela mutsalole akuba awo

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn 22 дня назад

    Iwe hule iwe ukangopanga masewela uzawona

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 22 дня назад +1

    a mec osadzalora kupanga chibwana kut wina akuguleni AYI
    otherwise tizavotaso kawili

  • @JamesDaud-jz7uq
    @JamesDaud-jz7uq 22 дня назад

    Chisankho sayesera kumeneko ndi kuba kodi ziyamba Chaka chino zimenezi Koma Bon kalindo akamayankhula musamazitenge Ngati ndiwamisala,,,,Koma Chalakwe

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 22 дня назад

    Kuyesela ku vote 😂😂😂😂 tikayesera PA ndani za ziiiiih

  • @emmanuelchimela4656
    @emmanuelchimela4656 22 дня назад

    Anthu asalole izi pakuti ife makani wina azichita kulawila

  • @MariaButao
    @MariaButao 21 день назад

    Pajatu bon ananena kale kuti kuyeselelako afuna abere anthuwa...zodabwitsatu zitsankho amayeselela???chonde amalawi umphawi watikwana osapitako kuzitsankho zoyeselela akavote onkha

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 22 дня назад

    First to comment ❤ Brian Banda moto 😊

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 22 дня назад

    Iwe mtali manja usamalize ndi maprogram akowo, unavapo kuti zoyetselera mavote

  • @user-eq8hr8li8h
    @user-eq8hr8li8h 22 дня назад

    Kuyesako anthu adzikavotera ndani?

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 22 дня назад

    Ndpo inagwa ndege ya iye chikangawa aMalawi akanasangalala..pano chili kwa papa kukamugwadira

  • @FleasherIshmael
    @FleasherIshmael 22 дня назад

    Musamaletu mayi mpinganjira amalawi siwopusatu

  • @MathiasEgama
    @MathiasEgama 22 дня назад

    Ndili ndi Funso,Kodi mukakhala pa mupikisano ndiye wina akuyamba kutukwana,chimathandauza chani ???? Answer me please

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft 21 день назад

    Ma vote sayesera

  • @moosamlembe3939
    @moosamlembe3939 22 дня назад +1

    Kodi basi malawi atsegulira ngozi za ndege?😢😢😢😢😢😢

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 22 дня назад

    Boba liziyesesa anthu akumudzi akuvutika

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 22 дня назад

    anthu awa akufuna kubela koma sayezera kuno kumalawi zibwana zimenezo muwona anthu apite kumeneko ndi mbunzi kwabasi ndipo kuyesera uku kubera munja chaka chamawa munthamanga inu ameke

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 22 дня назад

    😢😢Athu adakavutika madzi eeeeeh koma malawi

  • @SaeedMaunde
    @SaeedMaunde 22 дня назад

    A mec samalani kayetsedwe ka chisankho posakondela mbali otherwise any mistake zizayambitsa nkhondo mu dziko lathu n you will be answerable!!!!!!

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses 22 дня назад

    Ndipo sizinachitikepo kuyetselera mavote mu mbiri yathu muno malawi.

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON 22 дня назад

    😂😂😂😂😂 kuti mudzaphatikize ndi mavote a mr chikangawa yooo

  • @MatthewsJanuary
    @MatthewsJanuary 22 дня назад

    Ngati kuli kuyeserera yesani anthu 100 okha,osatizimene mukunama apazi

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 22 дня назад

    Aziyesera zichani chibwana chimenecho osangoyesera iwo okha mma ofesimo bwanji mpaka kuyesera malo 100 aaaaaaa

  • @user-sh5wq4uf6r
    @user-sh5wq4uf6r 22 дня назад

    Kuyetselela zitsankho zimenezo ndizoona? Mmm kumalawi ndikovetsa chisoni

  • @PanganoChilambe
    @PanganoChilambe 22 дня назад

    Sure mungakambe muyesa machine ameki muziyakhula ngati enanso anapita kusukulu osamakamba ngati muuza ana akalasi wani kuti nonse mwakhonza mwamva

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 22 дня назад

    Imeneso nde yiti,,,,kod zoyesedwa zabwera ndindani??? Zachanba akufuna kubwera agalu amenewa

  • @AREFRIEDNELSON
    @AREFRIEDNELSON 22 дня назад

    😂😂😂 makhwara kulibe muzipatara nde athu azitani ngati mukuligulitsa mankhwara afake vuto ndi utsogoleri ukungo baaa nde zili bwanji muzipatara

  • @WillmotChiuimia-vr6ou
    @WillmotChiuimia-vr6ou 21 день назад

    Kodi mavotiso amayesereraso? Aaa koma ndiye kubatu uku eshiii ineso ndakayika ndithu

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 22 дня назад

    Zisankho mpaka kuyetsera kae mmm kubera mavoti uku.

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 22 дня назад

    NDIPO NAWO AZIPANI ZOTSUTSA AKANGOYEREKEZA KUVOMEREZA ZOYESERERAZO PAMENEPO NDI PAMENE ATATHERE AWA ASANAMIZE A MALAWI ZISANKHO SITIMAYESERA KUYAMBIRA KALE ZITHEKABWANJI LERO NDI LERO CHONDE INU OSUSA BOMA MUSAVOMEREZE ZIMENEZO MUKANGOVOMERA MWALUZIRATU 2025 ISANAFIKE

  • @luckymalata3387
    @luckymalata3387 22 дня назад

    Kwa nsundwe kulibe mazi timamwa apazithaphwi

  • @JeanfatsanJere
    @JeanfatsanJere 22 дня назад

    Palibe zimenezo muziyeserela chani anthu inuyo musalore izi zisachitike akufuna zitheke zomwe anakoza a MCP

  • @user-en6mq4vx1d
    @user-en6mq4vx1d 22 дня назад

    Kuyeselera eti ai zikomo

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 22 дня назад

    Koma ma camera tameyesetsani ku times uko

  • @user-pf5er7gc9s
    @user-pf5er7gc9s 22 дня назад

    Zisankho zinayamba zayesedwa ? Izitu zofuna kusamalanazo izi

  • @ZekezekeNjala
    @ZekezekeNjala 22 дня назад

    Mundegemo amomaona ngati munali manganya

  • @JonathanMunthali-n3c
    @JonathanMunthali-n3c 22 дня назад

    Ukhuluku basi dziko lapansi nkoyamba kumva zoyesera utambwali

  • @MoosaChirwa
    @MoosaChirwa 22 дня назад

    Kodi kuyeselerako osamapanga nokhanokha ogwira Ku MEC konko bwanji mukufuna kuyesa dziko lose game yanji musewera Kodi

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 22 дня назад

    Dpp ikapusa ayibela mavoti for sure

  • @LasieMolebatsi
    @LasieMolebatsi 22 дня назад

    Ife zimenezo ayi

  • @GeoegeGRSHala
    @GeoegeGRSHala 22 дня назад

    Mwachita makora kupanga test pankhani yachisankho than Kuti mukozgane naamadam tepex

  • @MosesMkandawi-e2v
    @MosesMkandawi-e2v 22 дня назад

    Zonsezi zikudikila Peter muthalila osati gwape uyu alipoyu ayi uyu kwake ndi Kuba
    Basi demon

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 22 дня назад

    Amayi Ntalimanja zomatiyesa ife ayi

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 22 дня назад

    Paja chakwera ngwa satanic mmene zayambira kugwa ndegee zizingogwa basi. Chifukwa analowetsa kale ziwanda mdziko..chibusa choipa

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 22 дня назад

    Zinayambaso zachitika kuti zoyesera zisankho apposition osalora zopusazo akufuna kubera agalu awa

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 22 дня назад

    Koma plz chikangawa party wat au trying to play,,tangotulutsani report iyaaa

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 22 дня назад

    Koma kuba kwake zakuti zomayesela machine fodya et

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 21 день назад

    Anthu amaba koma or wakubayo yekha adzadabwa kut sakuwinabe 😂😂😂

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet 22 дня назад

    Chikangawa mashende yake

  • @Yoxym
    @Yoxym 22 дня назад

    Koma kumwera kuno why😭😭😭😭😭🇲🇼anthu akuchita kumwa madzi apachitsime koma boma kungoti zii ayi mutifuna nthawi yamavoti

    • @SteveriaNyalugwe
      @SteveriaNyalugwe 22 дня назад

      Ndipo zaka zammbuyomu madzi samkavuta kwambiri koma litalowa boma ili linasintha mapaipi kuwapatsa mpata a waterboard akuti cholinga anthu akumudzi asamangomwa madzi aulere adzilipira pakutha pamwezi. Lero anthu akuvutika kowopsa chifukwa cha zimenezo. Akanachotsa zimapaipi zawozo ndikubwenzeretsa zakale zomwezo bwenzi anthu asakuvutika ayi

  • @JosephyMakunganya
    @JosephyMakunganya 22 дня назад

    Chakwera paja he says Alowaso Boma ,Why he has confidence????

  • @KalipentalaJamu
    @KalipentalaJamu 22 дня назад

    Osalola ayi

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 22 дня назад

    Iya mwasitha kuti chani sizinachitikepo izo mukunenaizo ayi mukufuna kuti akawina pita muzamuphe ayi mwarephera

  • @MosesMkandawi-e2v
    @MosesMkandawi-e2v 22 дня назад

    Musalore anthu wotsutsa kuti ayeselele chifukwa akupwetekani futi samayeselera PA munthu ndee Amec ndi chakwela Ali PA ubale pobeal zisankho chonde a opposition Musalore kuyeselera ayi mapeto ake muputa mkhwiyo WA a Malawi wochuluka

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w 22 дня назад

    Sizithekha masankho sayeserera mwauponda

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p 22 дня назад

    Zisankho amayeserera???? Kuba masana

    • @EugeniaNgoyi
      @EugeniaNgoyi 22 дня назад +2

      Zija ankanena born kalindo zija zoti abweretsa machine anew cholinga chaka chamawa azizati ena anavota kale. Agalu amenewa

  • @MaryJefry
    @MaryJefry 22 дня назад

    Masankho amaeseredwa?zakuba basi

  • @phillkaunda5623
    @phillkaunda5623 21 день назад

    This is a lie. The new already how to say to the citizens

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 22 дня назад +2

    No Tpex please

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 22 дня назад

    Izi za testing ndizachamba kwambili wy a position alora zimenezi guy's aamcp azapweteka zipani zina akufuna kubera awa

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f 22 дня назад

    Tangotsegulani kawundula olembetsa osati zomwe mukunena apa zoyesera.
    Maina omwe muyeserawo mutani nawo?
    Please ngati mukupita kuma church pangani chilungamo for the first time