Ipondeni fadah ife timakupasani ulemu pot nanuso ndi freedom fighter God bless you mumatiziwisa zot sitimaziwa kuphatikiziraso apo chomwe muziwa ndie kukamba chilungamo chokhachokha
...Malawi constitution has a loophole in the law about crossing the floor. We are not matured enough in this kind of politics. "Dictatorship is the best form of democracy in Malawi". I deliberately put these two systems in quotes. Follow the American, British and South Afrikan systems when it comes to Parliament and Congress. You will find that Malawi is a Monkey system. Bingu wa Mutharika is the only leader, unfortunately we lost him prematurely, but that man deserved 30 years in office. Even more.
Kalindo and Suleiman respect to you guys
Am with you braz
Ulemu wanu boss
Kalindo ayi man aaah
Zaku sebia kalindo ananena kuti akukapanga ma passport 🔥🔥
Devil is a liar, and God is in control
Number one Channel
Suleman our super hero
God bless you brother
Thanks for the video we have been waiting for this boss continue to give us the best analysis
We always respect you boss
Proud of you our loved member of parliament Mr. Suleman
Kalindo anakamba kale izi big up brada
Thanks for your information we like u
Kalindoooo anatuuza kale
Suleman amadana ndizopusa kwambiri simunthu wamba zomwe akuchita chakwera ndigulu lake Mulungu awaone mwapaderadera live from Mozambique ❤❤❤
all on point brother
Respect elder ❤❤
You are the salt and the light, chosen and peculiar . Stay Blessed 💕
Best Chanel, ineyo ndikamava za chakwera ndimanyasidwa kwambili
Following from kwaNyamata ku Mbayani.
Born kalindo ndyamba kumukhulupilira ❤
Kalindo ayenela kukhala plezident of Malawi chifukwa amaona patali
Ipondeni fadah ife timakupasani ulemu pot nanuso ndi freedom fighter God bless you mumatiziwisa zot sitimaziwa kuphatikiziraso apo chomwe muziwa ndie kukamba chilungamo chokhachokha
Mesa Kalindo mumawona ngati wachamba.....lero ndi iziitu,,,age bill, Suleiman, etc. I like the analysis bro
Ndiye zonsezi akupangazi kuoezeke kuti mcp yawinaso ndiye tizakhale cheteso amalawi? Mmmmm kunena zoona moyo ukuwawa l don't think winawake angadzuke lero ndikuvoteraso mcp, koma ngt ingawineso mcp akuluakulu titha psitii, funso mkumati nduchifukwa chani amalawi timasakha kudekha kwambiri ndikumangodandaula muma social media? Nanga ndichifukwa chani apolice athu nawo akuvutika koka akulolera kuchitila nkhanza amalawi amzawo yet ufulu omwe akumenyerawu nawoso uzawapindulira? To be honest dziko lathu lafika ponvesa chisoni kwambi palibe department ya boma yomwe ikuyenda, kuakhala kunamizidwa ndiye tonse dziko muno tunamizidwa ndi omwe amazitenga kuti iwo ndi ophunzira omwe, but why malawi.
Amalawi anzanga a electrol commission akazangoti MCP yawina chisankho ziwani kuti abera chisankho. Thanks my brother poulula za agulugunyinda Nick ndi vitumbiko pofuna kuzabera zisankho apatu nkhanga zawona.
long live suleman . bakili muluz TV mbambande
We feel proud of you big man!!
Thanks u very much big boss
Whole respect to you brother God bless you.
Chanel ichi chili super ndpo number one❤
I like this channel
Good work big brother
Angotimalizamo mudziko muno😊
Excellent sir ❤❤❤
Thank you for your information Sir, chakwera mapazi ngati chophulila chipisi nkhungudzu wongofuna kuonanga miyoyo ya malawi
Keep up 💯 kalikose tikaziwa
Proud of you boss
Thank you for giving us good analysis
Inuyo man ndi born kalindo God bless all of you❤❤❤❤
Wamisala anaona nkhondo, respect to Suleman
Respect boss
Where do you get this information, you're the best 🙌🙌🙌
Ulemu wanu big man
Ur best man all the time ❤ brother
Watching from Israel kumunda
I like that guy because of his fearless
Amalawi tili nditulo kwabasi Chakwera ndi family yake akanakhala kuti akulamulira south Africa bwezi atawanthamangisa kale.
You are very correct
Respect to The DC, Respect to BK TV, Respect to all malawians who we are suffering
Now I can relate kalindo ananenaxo Zoti mwana wa chakwera wapita ku sebia weeks ago in one of his audios
Always open our eyes bro big up awululen basi
Amwene dzikoli tikukanda osatisewelo😊
Suleman your are good guy god bless you
❤❤❤timakunyadila kwambiri
Yes deal ya ma passport nd ma id the DC ananena kare
Zoona koma anthu amatsutsa the dc🔥🔥
President garu one day is one day manyero pa make chakwera
Uli ndimwai ulibe omako chifukwa mbuli kumalawi ndi satanic amatukwana omao Ngati nyani iwe
Your are best brother ❤️
Uli bhoo
U r always the best
Number one sir
Continue brother exposing these thieves
Big tv
Koma chakwera dziko walitenga ngati ndi village bwanji
Big boss
Number 1 channel ❤
🔥🔥🔥
Awe people of Malawi you have seen hell you never see before, 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
❤❤❤
ndi chifukwa chake Malawi ali pa umphawi wazawoneni because of this heartless people all behind chakwera
Mbambande bakiri muluzi tv
watching from Bagamoyo pa Boma
Zoti a dpp athibulana simukambako
Chilungamo chimawawa ndipo amvere izi basi kuti asithe
Koma chi president ichi!!!!!! Disgusting.
❤ Respect to Suleman
We need implacable politicians to represent Malawians in various strategic positions in our country
Mavoti a2025 Ngati ameki anganene kt Chakwera awina ndibwino kuzayamba nkhondo basi
Awina chisango anyani awa
Mumatiimila man.
...Malawi constitution has a loophole in the law about crossing the floor. We are not matured enough in this kind of politics. "Dictatorship is the best form of democracy in Malawi". I deliberately put these two systems in quotes. Follow the American, British and South Afrikan systems when it comes to Parliament and Congress. You will find that Malawi is a Monkey system. Bingu wa Mutharika is the only leader, unfortunately we lost him prematurely, but that man deserved 30 years in office. Even more.
Analankhula kale Kalindo zagalu awa zokhudza ulendo wa ku Serbia
Am first person to comment
Achakwera muthu opusa ndithu.
Bakili muluzi channel ❤❤
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
😂😂😂😂😂 kugula feteleza kuchipata iiiiii
Kalindo siwamisala
❤
Akufuna kubera zisakho
Posachedwa Mulungu atiyankha pakuti akumva kulira kwa a Malawi Osauka 😢😢 Eish!! Koma Bambo Chakwera mutivulaza ndithu
❤❤❤❤❤❤❤❤
The DC ananena kale
😢😢😢 Mavuto alipo
Simwawona
Shaaa
Kumalawi tidakaginabeb esh nkhondo Bas kazabwera chisakho
Chakwera President wamatudzi kwambiri. Basi dziko la Malawi lasanduka munda wawo oti adzichita zomwe akufuna zoona?
Respect 🙏
big boss
Tafotokozako ya culture Joseph hill
Mutu wanga sumayenda mkamamva izi😢
Every one knows now that malawi is going to right direction
Zingatikomele kutizikolathu KUTI MULUNGU ATIYIKILE MUTENDELA
Mumatha bigman.Nanga zakuthawa kwa a Paul mphwiyo zilipati?
pamenepa amalawi osagona tulo mcp ikupanga zinthu zoti azabere zisankho 2925 koma mukabera zisankhozo muzaoona nyekhwe kwambiri ndi amalawi chifukwa amalawi ndiokwiya ndi chakwera pa zimene akuchita anthu atopanaye chakwera