ZISAKHO ZAKU MANGOCHI ZODABWITSA ANTHU🙌🙌

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 15 окт 2024

Комментарии • 125

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 2 месяца назад

    Zomwe mwachita ndi a mec anuwo taziziwa mai uyu sitikufunaso

  • @Al-BaakirBoysSecondarySchool
    @Al-BaakirBoysSecondarySchool 2 месяца назад +7

    Congratulations to the MCP Counselor. We'll meet again in 2025.

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika 2 месяца назад

    Zaziiic see you 2025

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад +1

    Opposition yonse ndiyatulo MCP sitikuyifuna ikutizunza lero mukulola MCP kumawina kudera kwanuko

    • @MasterBlack-r2n
      @MasterBlack-r2n 2 месяца назад

      I wonder why? ngat kuli kubera ma vote, Shem on them wokubawo. ngat zachitika mu chilungamo, Mmmmm dziko Lili mmavuto. ndipo dziko lilipamoto

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад +1

    Anthu akumangochi ndiatulo mmene MCP ikuzunzira anthumu inunso zoona kumavotera MCP? Fertilizer lero alipantengo wanji thumbs la Chimanga liri pantengo wanji zoona kumavotera MCP anthu simuchedwadi kuyiwala

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 2 месяца назад +3

    Opposition kungona kwambili,ndipo zikuoneseratu kuti ngakale zisankho za president mcp ikumenyani m'mimba masoanu😮 ali zwiiiii......

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад +1

      Awuzeni asiye zotukwana zija koma ngati ndare zawo ndizomwe zija ayi azaluzaso ndithu chifukwa kutukwana kuja sikukopa anthu koma kuchosa anthu muchipani

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka 2 месяца назад +5

    Ndale sapangila pa social media...

  • @SababaHotel
    @SababaHotel 2 месяца назад +1

    Mayi awa masiku awo asala pang'ono

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 2 месяца назад +2

    Aaa apostion ake zisiru zokhazokha zongo songana bola Yomwe idali 2019 idali yochenjela 😭😭😭😭😭

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto 2 месяца назад +1

      Ndipo kwambiri chitsilu za anthu

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 2 месяца назад +1

    Muzimayi uyu achisedwe ku mec abera chisakho MCP singawine

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      @@marryphili5419 pitani ku police mukasume kkkkk

  • @SababaHotel
    @SababaHotel 2 месяца назад +1

    Zausilu kumangochi angawine wa mcp

  • @SababaHotel
    @SababaHotel 2 месяца назад +1

    Mangochi yinali kale

  • @PinDoor-pn3qc
    @PinDoor-pn3qc 2 месяца назад +3

    Nooo MCP siingawine M'mangochi zosatheka zimenezo

  • @ErnestLombola
    @ErnestLombola 2 месяца назад

    Mpira ndi pa ground osamaka pa social media

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 месяца назад +6

    Mwabera amcp simungawine kumangochi agaru inu

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 2 месяца назад +6

    Mukhalira yomweyo yoti tionayo paja tidakuuzani kuti pa u tube sipopangira ndale mukadaluzabe mcp woyeeeèe

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      Woyeeee❤❤

    • @Rometcma
      @Rometcma 2 месяца назад

      Dr Chikangawa woyeeee😂😂😂😂😂

    • @MCAnthonyNdau
      @MCAnthonyNdau 2 месяца назад +1

      Auzeni akuona ngati tonse tingakhale osutsa boma

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 2 месяца назад

      ​@@MCAnthonyNdauanthu akupha inu mubera mpaka liti

  • @chisomokawotcha1766
    @chisomokawotcha1766 2 месяца назад +4

    Zitsiru ndi otsutsa afuna anthu oti si achipani chawo awamenyere nkhondo paokha ayi musamale 2025

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 месяца назад +1

    I like the last part of the interview, that's the truth.
    Ndiye iweyo WA MCP usapuse nkumaona ngati Mangochi ndiya MCP udzakhumudwa kudzisankho za president and MP

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 месяца назад

    Koma nonse mukuyamikila mcp mutumbo mwanu ndithu mulibe chisoni ziko likiyendelamu

  • @Rometcma
    @Rometcma 2 месяца назад +1

    Malawi gradually is getting finished via MCP into dictatorship and zisankho izi opposition phunzilanipo kanthu and wake up Dpp anthu akuvutika.

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 месяца назад

    Chakwela palibe amene akumufuna or madela onse awina bwanji zaugalu

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 месяца назад

    Bread alipakhosi pa anthu amec

  • @lyfordnandolo4870
    @lyfordnandolo4870 2 месяца назад

    All the best cu there

  • @Shariffsa
    @Shariffsa 2 месяца назад +2

    Ukhatsala siwu president guy's

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 месяца назад

    Muzilamulila mpaka kutha kwadziko zaugalu

  • @GrantYohane-zd4qy
    @GrantYohane-zd4qy 2 месяца назад

    Nanga poti za unzikazo sizikutulika amene alibe muwataniii?

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita 2 месяца назад

    Tamva alankhula a mec iweso ukuwongezera

  • @BlessingsMpondaphiri
    @BlessingsMpondaphiri 2 месяца назад

    Zisiru za anthu mpaka kubera zomwez

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 2 месяца назад

    Zokomela nawe ukulengezawe amaiako osati amalawi

  • @GabrielSabudu
    @GabrielSabudu 2 месяца назад +3

    Zopusa dikirani tione a must 2025

  • @RhodrickMataya
    @RhodrickMataya 2 месяца назад +2

    Mayi opanda nzeru uyu Mulungu amuone mwapadera

  • @AmusedDimSum-hd5yp
    @AmusedDimSum-hd5yp 2 месяца назад

    mwabela ndiye mukuthokoza ndani

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 2 месяца назад

    Atupele ,apm chihana ndi utm onsewu ndi atulo ndipo MCP yabayadi mmimba

  • @lightchimbalanga
    @lightchimbalanga 2 месяца назад

    Malawians cannot be fooled by mere political rhetoric muzingochedwa nkumatukwana mcp pa social media malawians know what is right

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 2 месяца назад

      Nde you’ll know what is right ikazangowinansotu 😂. Ngt uli wanzeru you shouldn’t take it lightly

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 2 месяца назад +3

    Why ku mec mostly top officials are women?....fishy

    • @montfordkaulesi223
      @montfordkaulesi223 2 месяца назад +1

      Easily used materials

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 2 месяца назад

      @@montfordkaulesi223exactly. It’s rare to see women who are not moved by anything else but stand for the truth. God bless them

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi 2 месяца назад

    Sitikuyembekezera khansala ife koma president, akhoza kuwina khansala wa mcp koma apm ndikuzatenga boma.

  • @KingsleySitima
    @KingsleySitima 2 месяца назад +1

    Agalu amnewa afuna atiphese ife lelo mcp yawina chisakho Cha makhasala xmwe ife amalawi sitikugwilixana naxo

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      Ukati amalawi ineyo undichosemo chifukwa ine ndugwilizana nazo 😂

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 2 месяца назад

    Kmaso agalu inu a MCP Sizitheka zmeneso mwanya

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      @@Freedomchennl47 zikuwani ngati agalu achiwewe mukhalila yomweyo tuuu kkk

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад +1

    15:33 15:33 15:33

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 2 месяца назад

    Iwe ndiwe galu pamodzi ndi makolo ako

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r 2 месяца назад

    Ndi nzimayi so sindikukayika mpang’ono pomwe kuti ngwamabodza

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 месяца назад +1

    Mwabera agaru inu

  • @SpajazRaheem
    @SpajazRaheem 2 месяца назад

    Zikuwawani ndipang.ono apa tikumenyani 20205

    • @SolomonBewula
      @SolomonBewula 2 месяца назад

      Mmmmmm malume Poland moto munkhumudawatu paja mumapenhatu wakukhoti

  • @selinaSingini
    @selinaSingini 2 месяца назад +1

    Inutu mzingotukana pa social media azanu akugaya mcp mpaka 2030

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      Srs atitukwana zawozo azawo akupita chisogolo

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 2 месяца назад

      ​​@@NancyNyirenda-v9owhatever you saying one day you will be amazing mcp out of the country

  • @GOMEZGANIMPHAMBA
    @GOMEZGANIMPHAMBA 2 месяца назад

    Zachitika zimenezo oro mungakwiye motani MCP yawina basi😅😅

  • @morganchisama7464
    @morganchisama7464 2 месяца назад

    Asanyadire makhansala kuti awina adikire next year

  • @HalimaShafie-o7g
    @HalimaShafie-o7g 2 месяца назад

    Mcp ndiyakuba komaso achakwera anabela kaleso agalu awa

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 2 месяца назад +2

    Kupwambwana utsusa boma timing kulephera kukuchenjezani osamva chihana peter atupile nonse agalu zisilu asagolili iwalani zozawinaso

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 2 месяца назад

      Size makape a opposition ali pheeee

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba8394 2 месяца назад

    muli kungowawata pasocial media wosavhota ma stuctures paground zipani zanu zilibe muwina bwanji

  • @JamesUmali-p3e
    @JamesUmali-p3e 2 месяца назад

    Zizingatheke kwathu

  • @SpajazRaheem
    @SpajazRaheem 2 месяца назад +1

    Mcp moto kutibuuuuu... kkkkkk

  • @GrevazioManyozo
    @GrevazioManyozo 2 месяца назад

    Chitsogozo chabwino chikuoneka

  • @SpajazRaheem
    @SpajazRaheem 2 месяца назад

    Ifetimanziwa kutiawina a m cp basi

  • @KhalideNerve-mu1eq
    @KhalideNerve-mu1eq 2 месяца назад +2

    😮😮😮😮😮😮😮😮

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад

    Awadi ndi anthu opusa kwachenjeza ayi azanong'onedza bondo 2025 mcp izawinanso a chihana apeter atupele mukugona kwambili muchenjele

    • @EllinaBitto
      @EllinaBitto 2 месяца назад

      Ndipo inu A Chilima inuuuuuuuuuuuu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @KassimWilson-o8h
    @KassimWilson-o8h 2 месяца назад

    😂😂😂😂😂 zopusa

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 2 месяца назад

    What i know that Malawian is the people's you won't understand them i know and i believe that the votes mcp and you will see crying what the votes for

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 2 месяца назад

    Abela inu

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t 2 месяца назад

    Za ziiii

  • @Aubiekenneth
    @Aubiekenneth 2 месяца назад

    Abale mungovutika mcp singaluze or galu atayamba kugona mnyumba sizingatheke

  • @augrinngunga8031
    @augrinngunga8031 2 месяца назад

    Mukuzuza amalawi inu a mcp

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 2 месяца назад +1

    Abela

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад +1

      Apo àmaba inu munali kuti pitani ku police umbuli bas

  • @berthamigodi6529
    @berthamigodi6529 2 месяца назад

    Mcp is not on social media kkkkk muzingoziwa zotukwana pa social media azanu akujiya

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 2 месяца назад

    Chienjelani amalawi mcp mbava zohipa

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      Mbamva yayikulu ndiweyo paja musogoleli wawo😅😅😅

  • @JohnYoweli
    @JohnYoweli 2 месяца назад

    Kkkkkkklll😂😂😂😂😂

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 2 месяца назад

    ,unatani kukaberako nawe.

  • @ShearstonNyirenda
    @ShearstonNyirenda 2 месяца назад

    Mcp hoyeeeeeee!!!!!!!!

  • @WilliamBelvin-fq4ky
    @WilliamBelvin-fq4ky 2 месяца назад

    Chakwera oyeeeee

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 2 месяца назад

    Ku Bela ma vote

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 2 месяца назад

    Zokonyelela za mcp zopusa

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 месяца назад

    Opusa kwambiri ndi DPP

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 2 месяца назад

    Khansala si president

    • @lazaruschitsamba8394
      @lazaruschitsamba8394 2 месяца назад +2

      vhuto muli kungoyangula pa social media pitani mukavhote

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      ​@@lazaruschitsamba8394 eti inu mvutoso amawapopa kwambili ndi anthu oti sali kumalawi 😅

  • @captainmdima1102
    @captainmdima1102 2 месяца назад

    Mcp boma;!!!

  • @anoldkapolo4493
    @anoldkapolo4493 2 месяца назад

    Anthu adazindikira kuti pa RUclips ndipa anthu aganyu pomwe ife a mcp ndipa ground ndi zitukuko zomwe anthu akufuna. Tamuonani uyoyo wa ndale pa u tube Masaya ngati changa wagwa nayo ndipo mabwana ake amukwiyira. Zama yazi abwatusa. Mcp moto kuti buuuuu

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 2 месяца назад

    ???????

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 2 месяца назад

    Futsek

  • @AdamzChirwa
    @AdamzChirwa 2 месяца назад

    Mcp moto

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 2 месяца назад

    Dzisankho dzake dzamanyakadzo mcp dzimene yapanga pa Chilima ndindani angayifunenso,mwapatsidwa chibanzi a Mec inu.

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад

    Amalawi zoona mukuvoteraso mcp shame mkuyiona njara anthu akufa ni njara zinthu zikudura kwambiri bwanji tivotereko chipani china tioneko kuti zinthu mwina zingasitheko

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita 2 месяца назад

    Congrats to casual wa mcp

  • @JuliusSikamawawe
    @JuliusSikamawawe 2 месяца назад

    MCP moto

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 месяца назад

    Abela Mcp singawine ku mangochi

  • @juntoiman
    @juntoiman 2 месяца назад

    Ife Tikudikila bakili muluzi 📺 atiuze zenzen

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад +4

    MCP woooyee

    • @NancyNyirenda-v9o
      @NancyNyirenda-v9o 2 месяца назад

      Woyeèeeee❤❤❤

    • @Rometcma
      @Rometcma 2 месяца назад +1

      Dr Chikangawa woyeeee😂😂😂😂😂

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 2 месяца назад

    Mbava inu mwadya bazi agalu inu

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 2 месяца назад

    Zoputsa

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад

    Opposition yonse ndiyatulo MCP sitikuyifuna ikutizunza lero mukulola MCP kumawina kudera kwanuko

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 месяца назад

    15:33 15:33 15:33

  • @GeorgeTembo-v6i
    @GeorgeTembo-v6i 2 месяца назад

    ??????

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад

    Opposition yonse ndiyatulo MCP sitikuyifuna ikutizunza lero mukulola MCP kumawina kudera kwanuko