this is very educative i almost shade tears if we have parents guys lets appreciate and take care of them while they are still alive,they wont be with us forever that gesture of love and support to them is everything
Katundu wabwino uyu muli uthenga wa mphamvu.. Koma editor sanachite bwino in some areas,, too much long flashbacks nde zikumadzakhala ngati yayambilaso.. aaaaa satero. Chifupikitso chidzakhalepo in the next movie. Olo muthaso Kuyambila yomweyi kuifupikitsa. Koma luso lilipo ndithu, keep it up 😊
Ngati makolo anu alimoyo this is the right time to get more blessings from them by supporting them. Story yokhetsa misonzi iyi Continue resting in eternal peace my dear parents.
1. Flashback kuonelanso ngati movie yo tuoneraso kachiwiri. Next time osapanga zotere. 2. Kukula kwa mwana kukanakhala kumayambiriro, osati kutionesa mwana wakula kale ali pa ntchito, akunjoya ndi mahule then mpamene mukuzationesa mmene mai ake anavutikira nayo. Kutionesa kwakeso mongodzizimusa muja. Koma lesson ya movie ili super. Mawa ndiwatumizire fertilizer amai anga kumudzi.
Top Notch 🎉, Malawi we are on the right channel. We have something to be proud of and show to the world. Flash backs were unnecessary. That Gogo #Mavuto's Mother plz double her pay. She is talented
The story is quiet admirable keep it you, remember those parents you raise you up especially mothers, however , the too much of repeatition, and what happened after the mother calls the son..
This is good but the story should take 40min not 1hr plus because reputation of some sinario in this move which has taken almost 30min. That is to correct you but there is big lesson
Zomwe yapanga school days zija ivumbulutsa ma movie ochuluka...anthu inu mwakhala mukubisa ma movie anu I don't know why. Kumangotidyetsa ma trailers basi muli pheee. Otherwise thanks a lot for the upload.
mukuchulutsatu ma flashback, content inakutherani movie ya bho ngat iyiyi zoona mpaka kutioneretsa kawiri? why not including the burial ceremony instead of prolonged flashbacks?
iyiyi simayenera kukhara movie khani ili umu ndi 15 minutes chabe kwinakonse amakhara MA flash back bwezi ili episode 1 iyiyi or else khani mukanaikunga mwabho kuti inveke mwapamwamba otherwise uthenga ulibho
Dzikomo kwambiri mwasanja bwino story yanuyi ndaikonda. When coming back with yet another good play, minimise ma repetition, flashback isamatalikenso ngati real actioon. It was only 40 minute play. I hope you shall improve. Otherwise this is better coming , Malawi and keep it up guys
32:32 hapa ndio ufala yako ilianza, Mavuto. Ulinunulia mamaa mercedez pickup ya nini? Msichana unanunulia ka Suzuki Ignis and hauweki kwa jina yake. Mkiachana unachukua unatumia kama Uber.
😭😭😭😭 aaaaaa sad story but yophunzitsa i like this😭😭😭😭😭😭 God bless me i will never forget my parent...
this is what we call talent, KOMA MWACHULUTSA MA FLASAH BACK BOSS
This is a very good development anzathu ochita ma movies inu mutamapanga zoti azipezeka chonchi zikhonza kukuthandizani ndithu 👍
this is very educative i almost shade tears if we have parents guys lets appreciate and take care of them while they are still alive,they wont be with us forever that gesture of love and support to them is everything
Katundu wabwino uyu muli uthenga wa mphamvu.. Koma editor sanachite bwino in some areas,, too much long flashbacks nde zikumadzakhala ngati yayambilaso.. aaaaa satero. Chifupikitso chidzakhalepo in the next movie. Olo muthaso Kuyambila yomweyi kuifupikitsa. Koma luso lilipo ndithu, keep it up 😊
Ngati makolo anu alimoyo this is the right time to get more blessings from them by supporting them.
Story yokhetsa misonzi iyi Continue resting in eternal peace my dear parents.
Thank you so much
A nice story, I will never forget my Mum and Daddy 🎉🎉
Good reason to new generation 😢😢 we need to think twice before action, nice movie and its real story zikumachitika zithu ngt zimenezi
I mean, Good lesson
Thanks for the feedback
1. Flashback kuonelanso ngati movie yo tuoneraso kachiwiri. Next time osapanga zotere.
2. Kukula kwa mwana kukanakhala kumayambiriro, osati kutionesa mwana wakula kale ali pa ntchito, akunjoya ndi mahule then mpamene mukuzationesa mmene mai ake anavutikira nayo. Kutionesa kwakeso mongodzizimusa muja.
Koma lesson ya movie ili super. Mawa ndiwatumizire fertilizer amai anga kumudzi.
😅
Top Notch 🎉, Malawi we are on the right channel. We have something to be proud of and show to the world. Flash backs were unnecessary. That Gogo #Mavuto's Mother plz double her pay. She is talented
Very resonable movie i love it
Malawi now your acting very amazing big up the good work
Zokongola 🔥 🔥 🔥 tiyen nazo🔥✈️✈️
Anthu inu zikomo nkhani yanu ndizimene anandichita amuna anga lelo ana akula moyo unasintha ndili ndi nyumba yanga iiiiiii dziiko osamapangana chipongwe moyo unasintha tonse from L.L🎉🎉🎉❤❤❤
God is good anty 🙏
Let's share your experience call on 0999 713 665
Okay i will
Film was good and nice,
Powerful content delivered
Suggestion: flashback was too much
(Kuionera kuzaioneraso)
Yes apopo director sanapaunikile Bho
Thank you bossman
Tikuphunzira zambiri keep it up
Mmm this movie siyoonela anthu abp akhonza kupita wwa fresh Kuiwala kut ndi drama chabe😢😢
Never give up my bro
Thanks
So nice guys
Ndalira ine 😭🥲 continue
Is sad story koma ngati zitafika poterepa I never forget my parent ichi ndichibwana kkk ndiye chogulira bokosi lodula ndichaniii?
We Will be waiting for another part
But keep it up
Thanks
The story is quiet admirable keep it you, remember those parents you raise you up especially mothers, however , the too much of repeatition, and what happened after the mother calls the son..
Very good very good👍👍👍👍 thanks a lot
Amen
This is good but the story should take 40min not 1hr plus because reputation of some sinario in this move which has taken almost 30min. That is to correct you but there is big lesson
You right Broh
Truth
Correct
Fact
Film yanu yopatsa chidwi ndiyomphunzitsa koma kubwelezako aaaaa sizili bwino tikukhala ngati tikunena kawiri mobwereza
To the Video Team ur doing great ..... powerful message I really like it.......komano flashback was too much ......but nice Movie
Pakana ndangwesa tsozi pa film iyi❤❤❤
Makolo samayanhkula mwa natural,, amasonyeza kuti achita kukochedwa
Ndisewerotu ili amachita kulemba ndikukonza.
ma flashback mwaonjeza ma guy otherwise cool stuff
This is beautiful! But next time the flash back shouldn't be too long ❤
Wow nice story 😢😢😢🎉
Ma repeatation yapaka, the movie is so interesting
Film yili bho koma mwayibwereza kwambiri
Kukumbukira ngati mubwereza movie yonse
Beautiful lesson koma its like tubwereza too much flash back, but ili bho,keep up
Zomwe yapanga school days zija ivumbulutsa ma movie ochuluka...anthu inu mwakhala mukubisa ma movie anu I don't know why.
Kumangotidyetsa ma trailers basi muli pheee.
Otherwise thanks a lot for the upload.
Kkkkkk
Kuonela then mkuonelaso kachikena kamba ka ma flashback. Let's hope next will be professional
Ma Reparations yapaka,the movie is so interesting
Tamandani kapena kufanana ❤❤❤
Muli bhoo
I like it keep it up .
Content yabho kwambr
Km ma flash back samaenera kutero
This film is not well organized but still more I got my lesson..thanks.
This is nice...there is a lesson in it, but the flashbacks are taking too long, its like watching same movie twice....
But bravo
Zili bho
The fillm was supposed to be of 45 minutes
Sometimes, short and pretty professional is much better than repetition
eeeeee ndipo mayanga ndimakonda ndipo sindidzasiya kuwakonda mpakana kalr
Nice one
😭😭😭zosayeda
Nice movie
What a nice and touching movie
mukuchulutsatu ma flashback, content inakutherani movie ya bho ngat iyiyi zoona mpaka kutioneretsa kawiri? why not including the burial ceremony instead of prolonged flashbacks?
film yabwino koma mungobweleza zomwezomwezo bwanjii edting yanu inali motani
Kubwelezako ndi kuganiza zomwe zinachitika,
Move ndiyabwino koma yalakwika kwambir achulutsa ma flasah dzimatenga nthawi zobwerezazi plz next time muzatipatse zakupsa
Thumbs up
Edit it again, your flashback is just too much. 5 out of 10.
Next pls
iyiyi simayenera kukhara movie khani ili umu ndi 15 minutes chabe kwinakonse amakhara MA flash back bwezi ili episode 1 iyiyi or else khani mukanaikunga mwabho kuti inveke mwapamwamba otherwise uthenga ulibho
Eeeee film ilibwino koma kubwereza kwaojeza kuchotsa chidwi choonera
Dzikomo kwambiri mwasanja bwino story yanuyi ndaikonda. When coming back with yet another good play, minimise ma repetition, flashback isamatalikenso ngati real actioon. It was only 40 minute play. I hope you shall improve. Otherwise this is better coming , Malawi and keep it up guys
Thanks for the feedback
❤❤❤❤
Frash back plus reputation of words zachuluka komanso serios yoonetsa kut zithuzo zikuchitikad ikuchepa
Good lesson
Movie yophuzitsa kwambri iyi
Nyc
Too much flashback makes the movie boring
32:32 hapa ndio ufala yako ilianza, Mavuto. Ulinunulia mamaa mercedez pickup ya nini? Msichana unanunulia ka Suzuki Ignis and hauweki kwa jina yake. Mkiachana unachukua unatumia kama Uber.
Good movie but too much flashbacks.
Anyway keep up ❤
God bless all mothers
Km sinatisangalatse kumangobwereza pamodzi modzi
When will it be continued?
Will communicate bro
ikatero yathera pompa nde kumalawi kumeneko
Atsogoleri amove imeneyi akuyenera ayilingalirenso bwino Idzidzi asadzachiteso
Wow
km kulakwa kuliseza thembelero
Taphunzila zambili pitilizani
Thank you so much
The storyline is good and educative but the flashbacks mmmmh it's too much and boring. Next time edit
Ndipo anthufe timaphunzira mu zambiri AMBUYE MULUNGU WAKUMWAMBA akudalitseni
Please the story is good and acted well but very long
Mwangotibera basi filimu ya 30 mins kuonetsa nthawi yambiri kungochulutsa kubweleza, zopoira basi
The message is great, but editing yaonetsa umeana pang'ono.... too much redundancies
Ma flashbacks maonjeza and it's boring, koma story yanu ili bho
movie yabwino koma kungoyibweleza in the name of flash back. poor editing guys
Too much reputation but anyway movie ili mwala
Thank you
Too much flash back
The fillm was supposed to be of 45 minutes
Sometimes, short and pretty professional is much better than repetition