Nyimbo singawimise Muthu. ...koma all in all ilibho Ka bit Ko...koma zoti MCP izawinaso nde muiwale Ndalamazo kumadya or ine nkanakhala oimba ndikanapita konko😂
A simon ndi Kendal pajatu muli ndi ngongole ya 20 million ku Neef mukabweze naona chikalata chomwe munalembera a neef kt simukanisa kubweza business yanu sikuyenda
Chakwera my vote 🔥🔥🔥
My vote belongs to chakwera DPP Kagwere ukoo
Symon and Kendall ulemu wanu ❤❤❤ mwayipassadi moto tikumva kukoma boma ndilomweli,osusa ali mmazi, game yawakulira akulakalaka kuzisiya
More fire 🔥🔥🔥
Ndubwera kaye Ndukakoza ndikomenta mkamabwera
💃💃💃💃🕺🕺🕺 Chosinthila Boma sinduchiona because ku oposition kulibeko munthu wanzeru
Kulimbana ndi ana asatana kungotaya nthaw tiyeni timusiye mulungu amenya mkhondo tingovomerrza Mene zililimu Koma kutsogoloku mulungu ndiyemwe akudxiwa okonda nzake amatenga mavuto anzake kukhara ake ndye mulungu asamkha yekha
Nyimbo singawimise Muthu. ...koma all in all ilibho Ka bit Ko...koma zoti MCP izawinaso nde muiwale Ndalamazo kumadya or ine nkanakhala oimba ndikanapita konko😂
@@giftbanda7690 🤣🤣🤣🤣🤣 Koma ndaseka
🔥🔥🔥🔥
💃💃🕺🕺💃🕺 fumbi koboo!!!! BOMA NDI LOMWELI
Pepa malawi anthu akusapota mfiti ndalama iweyo anakonza
Oimbawa akungofuna adye nawo ndalama zama campaign.koma ozawavotela akuwadziwa kale
Kwachematu 🔥🔥🔥
❤mcp 2025 bomaaaaaaa🎉
nyimbo yabwino ndinthu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Mxeeew ndinu agalu kobasi
Nice
Mutchambwe song
Ine mphee ku ma stand
Ndetu chakwera wanuyo moyo wawora
Boma ndilomweli ,ku opposition kuli munthu okalamba amaona ngati amalawi ndife opusa eti aghona nyekhwe
Inuyo a kendal komanso symon mukusonkhezera kt dziko la malawi lipitilire kuzuzika chifukwa cha utsilu wanu kapena kt dyera lanu.
Mkono wina mwabisilanji chakwela
Koma ndrama anakoza😂
Anthu mukudya mabanzi
Kuimbila mmanja posayenela
Boma ndlomweri akwiya ndfiti
A simon ndi Kendal pajatu muli ndi ngongole ya 20 million ku Neef mukabweze naona chikalata chomwe munalembera a neef kt simukanisa kubweza business yanu sikuyenda
Ai zkm,,zilikoooo ,
Kwavuta kumalawi moti onse oimba angakhale opusa opposition mkumanda koma anyamata awawa adakonza bomaaa ndilomweli DPP ilikumanda zoona
😂😂😂😂
Pamtumbo panu bwaaaaa
Nduona ngat tisakwiye 😂😂
More fire 🔥🔥🔥