Sameer Suleman Lelo Chakwera Nde Sanamunyengelele Ndipo Amutokotela

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 дек 2024

Комментарии • 55

  • @WaysoLufas
    @WaysoLufas 11 часов назад +2

    Suleman ndwe mamuna ndpo uksnsngokhala presfent wa dpp

  • @AdamRobert-u9v
    @AdamRobert-u9v 55 минут назад

    Tiyankhuleni Boss Sameer, osatopa and osaopa Mulungu will still continue guide and protect you

  • @MalikKim-ni2ns
    @MalikKim-ni2ns 9 часов назад

    Mr president ❤

  • @FelixTsabolaNamaya
    @FelixTsabolaNamaya 10 часов назад

    This guys can be a good President, he is fearless.

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue 10 часов назад

    The guest honorl😂😂😂 kkkkkkkkk

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 11 часов назад +1

    Moto kuti buuuu ❤❤❤

    • @ChristinahNkwanda
      @ChristinahNkwanda 10 часов назад

      Mulungu Azikudalitsani mpaka
      Tiwinenso 2025 .GODBLESS ALWAYA PETER ADADI OYIIIIYEEEE.

  • @AlubiAsedi
    @AlubiAsedi 9 часов назад +1

    Km tu nde mwayankhuratu ee mulibe mantha kkkkkkkkk😂 ha km chinyamacho chichoke pampando basi sichoncho amalawi DPP OYEEH

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 9 часов назад

    😂😂😂😂 koma kumalawi

  • @praciouspiyo
    @praciouspiyo Час назад

    zowonad

  • @assyatujohn6264
    @assyatujohn6264 10 часов назад

    Koma i❤

  • @ShuxyStambuli
    @ShuxyStambuli 10 часов назад

    Ng'alura bas mwana wachepa ngazo izii

  • @WaysoLufas
    @WaysoLufas 11 часов назад

    Suleman umatha

  • @razackibrahim5880
    @razackibrahim5880 10 часов назад

    💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @EnerstMakwinja
    @EnerstMakwinja 11 часов назад

    ❤❤❤

  • @CharlesChingwalu-q9u
    @CharlesChingwalu-q9u 15 часов назад +5

    Big up sulemani ❤😂

  • @DrakLMalota-z5e
    @DrakLMalota-z5e 10 часов назад

    Machine truth always pain ndipo

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 11 часов назад

    Kkkkk malume akut yamanja amaionaso💪💪

  • @PATRICKTHIMZY-g1p
    @PATRICKTHIMZY-g1p 11 часов назад

    Kma sulemani kkkkkkkkkkkkkkk ulibe matha😂😂😂

  • @CharlesChibisa
    @CharlesChibisa 12 часов назад

    Zinangovuta you were supposed to be opposition leader. this man Sumeer Suleman was born to be a natural leader.

  • @PATRICKTHIMZY-g1p
    @PATRICKTHIMZY-g1p 11 часов назад

    Sulemani tikakumana ku paliament😂😂😂

  • @andexnjale1963
    @andexnjale1963 10 часов назад

    🏃🏃🏃🤸🤸

  • @HenzelMikolasi
    @HenzelMikolasi 11 часов назад

    God bless and protect you sir

  • @BensonJere-i9k
    @BensonJere-i9k 14 часов назад

    Kkkkkk😂😂😂😂😂😂 koma Suleman iweyo anakonza,, ndiye wati Chakwera or atalapa mulungu sangamukhululukire coz machimo afila kuposa kapezi" 😂😂😂😂😂😂😂

  • @andexnjale1963
    @andexnjale1963 10 часов назад

    Kodi Rambo akunenedwayu ndindan? 😂😂😂

  • @FlengieAustin
    @FlengieAustin 10 часов назад

    Mmmm koma yaaa

  • @NyuwaniMkwela
    @NyuwaniMkwela 11 часов назад

    Chikangawa uli bazi 2025

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 4 часа назад

    Makaladi sitiopa

  • @SharifWad
    @SharifWad 10 часов назад

    Umakwana

  • @EvansKachulu
    @EvansKachulu 14 часов назад +2

    Kod mkuluyu bwanji akulu akulu tingomupasa udingo wa Leader of opposition ku parliament cos ali ndikuthekela not chifukwa cha msinkhu koma mzelu zolankhulila anthu ake

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 13 часов назад

    Auzeni zoona achikangawa.

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 12 часов назад

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣malume suremani akulu awa English kulibeso koma bozaaa lirithoooo

  • @RodgersMwanakhu
    @RodgersMwanakhu 14 часов назад

    Iwe Suleman ndiwe dolo kwambiri

  • @Dellingsmunthali
    @Dellingsmunthali 12 часов назад

    Koma chonde musangonena awa tizawafinye kwambiri atitora kwambiri kumpoto fertilizer kulibe koma harayo kodi akuganiza chani??

  • @BensonJere-i9k
    @BensonJere-i9k 14 часов назад +1

    Kuyankhula straight wakwiya ndi mfiti,, chilungamo chili ngati kukuponda pa chilonda

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 13 часов назад

    machine❤

  • @MarvinDulani
    @MarvinDulani 12 часов назад

    Koma chilungamo eeeeee chimawawa eeeeeeeee Suleman ulingat ineyo sindingaope chakwera

  • @McshonWilliam
    @McshonWilliam 12 часов назад

    Chakwera watha bas

  • @stephankamyata3862
    @stephankamyata3862 11 часов назад

    Bigy waife wamu Hannover park😅

  • @MynessChirwa
    @MynessChirwa 13 часов назад

    😂😂❤

  • @RodgersNthengwe
    @RodgersNthengwe 12 часов назад

    Gud point not chikangawa

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 13 часов назад

    😂😂😂😂😂

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 13 часов назад

    Adpp fundo mulibe mmangolimbana ndi chakela ife sitingakusateni daily kunyoza mmene mnayambila muja .simnatope ayi nenani nfundo

  • @AlexanderMateketa-i8l
    @AlexanderMateketa-i8l 13 часов назад

    Suleman ndiwe katundu aise mcp ili kutali,, tili pa mbuyo pako.

  • @PempheroAlli-v8y
    @PempheroAlli-v8y 14 часов назад +2

    yakhulani bwana chakwera ndi galu,mbuzizo

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 12 часов назад

    Kape iwe mukufuna kudzabaso Dola ngati makape anawaso andare ndinu akuba basi ndarama mukufuna kungaira anthuzo udzabweza

    • @yasiniKalonga
      @yasiniKalonga 12 часов назад

      Inde amaba koma mavuto sanafike pachimake ngat pano

    • @EnifarSeleman
      @EnifarSeleman 12 часов назад

      Adaba kwanu chitsiru iwe

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o 14 часов назад

    Machini bwana❤❤❤ ulemuwanu

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 14 часов назад

    Suleman more🔥🔥🔥🔥🔥

  • @CharlesChingwalu-q9u
    @CharlesChingwalu-q9u 14 часов назад +2

    Rambo😂😂😂

  • @MaureenMaonga
    @MaureenMaonga 14 часов назад

    Mcp mbuzi zokha zokha. Mizimu yakwiya anthu sakukusekeleraso iwe chikangawa

  • @BashiruAdamus-l2b
    @BashiruAdamus-l2b 14 часов назад

    Sulemani uyu ndidolo

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga 12 часов назад

    Chitseko chapana a MCP