Nyimbo yabho my favorite inaimbidwa bwino komaso video quality koma chonde Akaziwo Azipanga Act mwa Gospel for the next tune Asakhale ngat ma model in the Secular Song iyiyi ndi Gospel aziilemekeza. thank you for the vibe God bless
@@rodrickmbulumbunde7394 zikomo kwambiri koma ngt mkotheka please mtayipanganso upload coz pa download sikutheka kupanga download HD video ikungolora 3gp.
maso ndi maso ❤
Zilibwino kwabasi 😊
Beautiful song
Nyimbo yabwino kwambiri my favourite
Powerful msg
❤📖
My favorite song
Always it Remains my Favorite 😍
My favourite ❤ 😍 💕
Wow👏 nyimbo yabwino, mavinidweso auzimu😍... i can't stop watching again & again❤🎉🎉💃💃💃
May God bless you and give you more talent to release another album nice
Nice brother's and sister's glory to jesus
Amen sister! Are you related to Joshua Kungwezo? If so, please pass our regards.
ruclips.net/video/Rh0r9tct5uA/видео.html
Nyimbo yabho my favorite inaimbidwa bwino komaso video quality koma chonde Akaziwo Azipanga Act mwa Gospel for the next tune Asakhale ngat ma model in the Secular Song iyiyi ndi Gospel aziilemekeza. thank you for the vibe God bless
Received with thanks. Tifotokoza maganizo anu. Thank you for the support.
Nice choir group... Which country?
Malawi
Thank you for your support
Malawi
Imodzi mwa nyimbo zomwe ndimaximonda apa mwamenya zamphamvu kobasi🥰
Zikomo kwambiri Mtsogoleri.
Beautiful song
Thank you
Amen
Amen
Beautiful singing 🙏
Thank you
Kuyimba koma uku osati dzina tikumaziwona ndi oyimb wena pitilizani kuyimba bwino ndithu zabwino zonse
Nyimbo yabwno kwambiri.
Tathokoza kwambiri and we need your support to spread the gospel of our Lord Jesus Christ. Once again thank you very much.
@@rodrickmbulumbunde7394 zikomo kwambiri koma ngt mkotheka please mtayipanganso upload coz pa download sikutheka kupanga download HD video ikungolora 3gp.