MALAWI WATHU
MALAWI WATHU
  • Видео 123
  • Просмотров 633 416

Видео

AKWENI ALAVULA PANO...?
Просмотров 2622 месяца назад
UTM,a Tonse Alliance partner with MCP has just announced that they are out of the alliance..watch the Press Announcement as it happens...
UTM YATULUKA MU TONSE ALLIANCE...Zitha bwanji ndi a Michael Usi?
Просмотров 2633 месяца назад
UTM,a Tonse Alliance partner with MCP has just announced that they are out of the alliance..watch the Press Announcement as it happens...
Osayiwara Kuti Zinayamba Bwanji?
Просмотров 3,6 тыс.3 месяца назад
We talk about the benefits of mines in Malawi and who are the beneficiaries?Does Malawi really benefit from them?
A PETER MUTHALIKA ASIMIKIZA KUTI AYIMASO || ZINTHU zakwera MITENGO chifukwa cha a CHAKWERA akutero?
Просмотров 5775 месяцев назад
Following the Peter Muthalika Rally in Blantyre at Njamba Park
Mabungwe Omwe Siaboma AKWIYA Ndikuthesedwa kwa Mlandu wa Dr Saulosi Chilima...Mverani Nokha!!
Просмотров 1,3 тыс.5 месяцев назад
CSO Press Briefing..
Dr Saulosi Chilima Milandu YATHA||TSOPANO 2025 ULENDO UYAMBIKE!!
Просмотров 3,1 тыс.5 месяцев назад
Malawi Government has just discharged all corruption charges against the vice President Dr Saulosi Chlima...We say this when battle for the 2025 General Elections starts!!!
A Chakwera Akuti Mabvuto tili Nao Ku Malawi ndi atempolare....Njala,Katangale,Zinthu kudura?
Просмотров 1,1 тыс.5 месяцев назад
We talk about the benefits of mines in Malawi and who are the beneficiaries?Does Malawi really benefit from them?
KODI A VAISI PULESIDENTI AYAMBA KUTUMIDWA NDI A PULESIDENTI CHAKWERA PANO?
Просмотров 11 тыс.5 месяцев назад
We talk about the benefits of mines in Malawi and who are the beneficiaries?Does Malawi really benefit from them?
KODI AKUPINDULA NDI MIGODI KU MALAWI KUNO NDI NDANI?
Просмотров 3945 месяцев назад
We talk about the benefits of mines in Malawi and who are the beneficiaries?Does Malawi really benefit from them?
Ambuye Mntengeni| Mowa Wachilendo Wagwedeza Mnzinda wa Blantyre|Anthu 8 Afa Kale...
Просмотров 1,2 тыс.6 месяцев назад
We are discussing the mysterious alcoholic drink which has caused 8 fatalities in Blantyre Malawi
Aphungu a DPP kukunthana mu Paliyamenti|Age Bill Yavuta!!!
Просмотров 2,7 тыс.6 месяцев назад
We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!
Mwina Tinayiwala Mmene Zinaliri 2019 Kuti Enafe Tilowe M'Boma?Kotsutsa Kutatiphweteka !!
Просмотров 3,8 тыс.6 месяцев назад
Chilima press briefing 20219..
A John Kapito Akuti Katangale Wanyanya ndi Boma la Tonse Alliance?
Просмотров 7 тыс.7 месяцев назад
We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!
Kamuzu Chibambo Kutsimikiza Kuti Tonse Alliance Sakudziwa chimene Akuchita|Amamangidwa Mmasamba
Просмотров 3,9 тыс.7 месяцев назад
We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!
Mmene a Tonse Alliance Akuthawira Kulephera Kwao Posintha Malawi| Kuloza Chala Ogwira Ntchito m'boma
Просмотров 2,8 тыс.7 месяцев назад
Mmene a Tonse Alliance Akuthawira Kulephera Kwao Posintha Malawi| Kuloza Chala Ogwira Ntchito m'boma
AKUSINTHA MALAMULO KU MCP CHIFUKWA CHAKULOWA KWA ULADI MUSSA M'CHIPANIMO?
Просмотров 2,6 тыс.7 месяцев назад
AKUSINTHA MALAMULO KU MCP CHIFUKWA CHAKULOWA KWA ULADI MUSSA M'CHIPANIMO?
Peter Muthalika KUZUZURA President Chakwera kuti Wasokoneza Malawi...Amuchosa Chakwera 2025!!
Просмотров 3,2 тыс.7 месяцев назад
Peter Muthalika KUZUZURA President Chakwera kuti Wasokoneza Malawi...Amuchosa Chakwera 2025!!
Kalanga Ife,Tithawira kuti?Akuti Namondwe Filipo Akuphikidwa pa Nyanja ya Indian Ocean Kubwera ku MW
Просмотров 2,3 тыс.7 месяцев назад
Kalanga Ife,Tithawira kuti?Akuti Namondwe Filipo Akuphikidwa pa Nyanja ya Indian Ocean Kubwera ku MW
Zayamba KUULULIKA ZAMALIFOMU ANAPELEKA CHILIMA kwa a PULESIDENTI
Просмотров 33 тыс.7 месяцев назад
Zayamba KUULULIKA ZAMALIFOMU ANAPELEKA CHILIMA kwa a PULESIDENTI
Mneneri Wakale wa MCP Wazomeleza kuti A CHAKWERA AKANIKA KUKWANILITSA ZIMENE ANAWAUZA A MALAWI?
Просмотров 9 тыс.7 месяцев назад
Mneneri Wakale wa MCP Wazomeleza kuti A CHAKWERA AKANIKA KUKWANILITSA ZIMENE ANAWAUZA A MALAWI?
MaBishop Akuti Utsogoleri Wa Masomphenya Kulibe ku Malawi|Akufuna Kutsintha 50%+1 Zikumveka Ngati?
Просмотров 14 тыс.7 месяцев назад
MaBishop Akuti Utsogoleri Wa Masomphenya Kulibe ku Malawi|Akufuna Kutsintha 50% 1 Zikumveka Ngati?
Kodi Aphungu Athu Amatiyimiladi Ife a Malawi kapena Zipani Zao?
Просмотров 1,3 тыс.7 месяцев назад
Kodi Aphungu Athu Amatiyimiladi Ife a Malawi kapena Zipani Zao?
Mmene Anthu awa Otchedwa 'OMENYERA UFULU' Amatipusisira a Malawi?
Просмотров 7 тыс.7 месяцев назад
Mmene Anthu awa Otchedwa 'OMENYERA UFULU' Amatipusisira a Malawi?
Mmene ANASAUKIRA a MIKE CHILEWE chifukwa cha Anthu Asanje ndi Andale!!
Просмотров 4,7 тыс.8 месяцев назад
Mmene ANASAUKIRA a MIKE CHILEWE chifukwa cha Anthu Asanje ndi Andale!!
Mmene John Tembo Anaphera Tsogolo La Kinnah Phiri Losewela Mpira Kunja !!!
Просмотров 5 тыс.8 месяцев назад
Mmene John Tembo Anaphera Tsogolo La Kinnah Phiri Losewela Mpira Kunja !!!
Mary Navitcha a DPP Kuyanka Zimene Anayankhula a Pulesidenti mu Parliament...Kusambwaza SONA !!
Просмотров 1,1 тыс.8 месяцев назад
Mary Navitcha a DPP Kuyanka Zimene Anayankhula a Pulesidenti mu Parliament...Kusambwaza SONA !!
A Malawi Ambiri Akuti a Chakwera Amangodziwa Kuyankhula Osati Kugwira Nchitoyo...Mvelani Nokha!!
Просмотров 4,2 тыс.8 месяцев назад
A Malawi Ambiri Akuti a Chakwera Amangodziwa Kuyankhula Osati Kugwira Nchitoyo...Mvelani Nokha!!
BREAKING NEWS!!! a ACB SANAUDZIDWE KUTI NDALAMA ZAPELEKEDWA KWA SATTAR?
Просмотров 2,4 тыс.8 месяцев назад
BREAKING NEWS!!! a ACB SANAUDZIDWE KUTI NDALAMA ZAPELEKEDWA KWA SATTAR?
Kodi a Nyuzipepala Apepesa Zokhuzana ndi Sattar ndi Boma kuti Contract Palibepo Yanyuwani?
Просмотров 8868 месяцев назад
Kodi a Nyuzipepala Apepesa Zokhuzana ndi Sattar ndi Boma kuti Contract Palibepo Yanyuwani?

Комментарии

  • @PatrickChilimba
    @PatrickChilimba 13 часов назад

    Malumewa amakwanira ine pastor chilimba chiladzulu

  • @BlessingsUndih
    @BlessingsUndih 8 дней назад

    Big Gwaladi zabhobho

  • @JacklineNiwahereza-ni3pm
    @JacklineNiwahereza-ni3pm 14 дней назад

    Mabotolo abwino kwambili he need government support

  • @leonardchikalogwe789
    @leonardchikalogwe789 16 дней назад

    0 pa 10 aaaa kukanika kifusa mafuso azeru ndithu shaaa

  • @IsaiasIsaias-yq7zg
    @IsaiasIsaias-yq7zg 21 день назад

    Kodi jogwaladi ndiwosauka?

  • @IsaiasIsaias-yq7zg
    @IsaiasIsaias-yq7zg 21 день назад

    Onanizimodzi inu kumanga nyumba ndi kodula koma kugula mowa ndikochipa

  • @IsaiasIsaias-yq7zg
    @IsaiasIsaias-yq7zg 21 день назад

    Kkkkk

  • @IsaiasIsaias-yq7zg
    @IsaiasIsaias-yq7zg 21 день назад

    Mbambande gwaladi

  • @KenvasBanda
    @KenvasBanda Месяц назад

    Zili bo

  • @JosephMisomali
    @JosephMisomali Месяц назад

    This is awesome, it's very good to check on pple whilst alive osat munthu wafa ndiye bas ma camera lendelende sizipereka nzeru

  • @Queen1984Banda
    @Queen1984Banda Месяц назад

    Washing from midland south Africa,nice program 😊

  • @ArafateDiquissone
    @ArafateDiquissone Месяц назад

    Amalawi mukavotera chekwela muthako kumneko.

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Месяц назад

    Ndipo osafowoka

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness Месяц назад

    Inuyo ya prensident mwakana kuti ndiyaboza ndiye sankhani inuyo ndakubanja ndimu zikufunikira

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness Месяц назад

    Ngati lipoti mukuyikana ndiye bwanji mupeze anu wofufuza tizamve lipoti lenireni

  • @AdsonPwele
    @AdsonPwele Месяц назад

    Kodi ku Malawi kuli anthu othani osekelera zoipa ngati chikangawa misozi iyi talira iphindura no matter what! God created man & watching

  • @AdsonPwele
    @AdsonPwele Месяц назад

    Moto unandi guys tilipo ife🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @ShadreckEliya
    @ShadreckEliya Месяц назад

    😢😢

  • @Cee_Busy_Mw
    @Cee_Busy_Mw Месяц назад

    Ticking

  • @AudtinEliya
    @AudtinEliya Месяц назад

    Gwarad unayamba Kare kuyimba Koma Roko nyuma eeeeeeee .umagura chiyani ndarama nzimene umapanga choooooo😢😢😢😢

  • @charlespeter138
    @charlespeter138 Месяц назад

    Kkkkkkkkkkkkk

  • @ElizaJoseph-q9w
    @ElizaJoseph-q9w 2 месяца назад

    Amunyanyiwa ntchito simuiziwa ayi mukulephera kumfusa mafuso mwaonongatu ndalama ulele

  • @XolaMzebetshana
    @XolaMzebetshana 2 месяца назад

    Komaso dzilikooooo

  • @RanneckKapata
    @RanneckKapata 2 месяца назад

    nice one

  • @FatimaSande-lb1hd
    @FatimaSande-lb1hd 2 месяца назад

    Chithandizo cho iye ndalama amapeza koma mowa aaaa..... Tazikhalani serious kuzolowera kupempha eti? 🤔

  • @FatimaSande-lb1hd
    @FatimaSande-lb1hd 2 месяца назад

    Kuyembekezera kuti ndimva funso loti joe ali ndi Ana angati? Ationetsa madam a joe ayi ndithu za ziiiii..... 🤭

  • @KilionSphiri
    @KilionSphiri 2 месяца назад

    Mfundo zikuwoneka zikuwoneka mulibe next time. Zafuseni zazeru . Komaso gwaladi mwatichitisa Mandyazi asa asa hiya

  • @LukaSpoko-i3l
    @LukaSpoko-i3l 2 месяца назад

    Akomaamakana ndipotimawanyadila

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 2 месяца назад

    Akamunaamenewo amativesakukoma jo

  • @RittoKei
    @RittoKei 2 месяца назад

    Is this comedy 😅😅😅😅

  • @LonelyKhoma
    @LonelyKhoma 3 месяца назад

    Gwaradi sakufunika kumupasa ndarama ayi kuthandiza kwake kuimirire ndi munthu wina azimupangira kaya ndi nyumba iyeyo akapeze yomanga kare ndikumuikamo mmmm zokhudza bwanji kuntchuka koseku 🤔

  • @SadguruPrernaTrust
    @SadguruPrernaTrust 3 месяца назад

    Jumping Jack !

  • @BrianNowa
    @BrianNowa 3 месяца назад

    Zopanda ntchito izi, anthu akuvutika kwambiri kumudzi, okalamba, aumphawi, olumala, amasiye, odwala, osamalankhula mwachibwana kut Mulungu Ali mbari yanu yet zinthu sizili bwino, kulankhula ngati anthu opanda mzeru, palibe chanzeru chomwe mukuchita chopindulira Malawi kuposa kumangomanga wanthu ndi kusintha maina azipatala zoti simudamange ndinu, 4 years just for nothing, shame on you guys, mzipatala mankhwala mulibe, chitetezo taaa, ma school Nde mwakweza ma fees, anthu akumudzi omwe alibiletu chiyembekezo ndipo alibe chilichose akwanitsa bwanji kulipilira Ana awo ma school, chakudya Nde kulibiletu, chomwe mukuganiza mkuti tidzadzitsa bwanji matumba wathu kuti tidzabele zisankho, AGALATIYA opusa, oyamba ndi zabwino kutsiliza ndi zoipa, When I said amalawi akuvutika I mean it, mukamadya bwino kumitundako musamati aliyese a kudya, go to the villages and see how life is, you will cry, anthu a kugona ndi njala and you are expecting those people to go and vote for you this coming 2025 nonsense, MAY The Soul of SKC continue to Rest well and hope he is watching you all,

  • @FwasanChavula
    @FwasanChavula 3 месяца назад

    Ufiti

  • @JaytuSaisi
    @JaytuSaisi 3 месяца назад

    amapanga sewero

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 3 месяца назад

    Kuyankhula koputsa kwambili,Kodi moyo ndi wanu??? Inu anthu omvetsa chisoni kwambili

  • @Cathy-oc7vd
    @Cathy-oc7vd 3 месяца назад

    It is supposed to happen.. MCP is a big party sangalore kuberekedwa

  • @KimuEmmanuel-lv9wt
    @KimuEmmanuel-lv9wt 3 месяца назад

    Chakwera ndi mbudzi yamunthu

  • @PercyTrading
    @PercyTrading 3 месяца назад

    Koma malawi kodi mukhalabwamji? monga azomba ndi azisuzo mumamwalila apanda kanthu kalikose.

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 месяца назад

    Mwagwanayo UTM yakutulukani forever Chakwela kwamai ako

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 3 месяца назад

    chisankho chabwino koma osanyoza adzanu ayi

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 3 месяца назад

    Chakwera ndi munthu olephela ....mkazi olanda amavuta

  • @PercyTrading
    @PercyTrading 3 месяца назад

    Anamangindwa chifukwa chani

  • @mannersaint
    @mannersaint 3 месяца назад

    Ayi ndth anthu matha kuvina eeeee😄

  • @OsmanOsher-sh6gp
    @OsmanOsher-sh6gp 3 месяца назад

    Osayiwala chipande ndipowomola

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 месяца назад

    Tso pali chimene wapanga chakwera success! Agalu achabe chabe.

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 3 месяца назад

    Za ziiiiiiii! Chakwera ndi MCP yake akagwere uko

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 3 месяца назад

    Zakuvutani bas

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 3 месяца назад

    2025 president wanu chakwela? Is so sad for Chilima 😢 rest well

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 3 месяца назад

    Ubwino simuvota nokha